Malawi VLOG

Malawi VLOG Welcome to Official page of [MALAWI VLOG]
For Entertainment, Education,
Exploring the Country(Malawi),
Sharing thoughts. Connecting People. RUTHLESS IDEALISTIC
(5)

promoting Music, Movie and Poems. CEO Chavula Nicklaus

Follow us Malawi VLOG
09/07/2025

Follow us Malawi VLOG

Opulumutsa(rescuers) ku Indonesia akufufuza anthu ambiri omwe asowa atamira pa boti pafupi ndi Bali .Gilimanuk, Indonesi...
04/07/2025

Opulumutsa(rescuers) ku Indonesia akufufuza anthu ambiri omwe asowa atamira pa boti pafupi ndi Bali .

Gilimanuk, Indonesia AP - Opulumutsa ku Indonesia anali kufunafuna anthu 29 omwe adasowa Lachinayi pambuyo pa boti litamira ndipo anthu asanu ndi mmodzi(6) adamwalira usiku watha pafupi ndi chilumba cha Bali ku Indonesia.

Mnyamata wazaka zitatu ndi amayi ake ndi omwe anafera pafupi kwambiri omwe matupi awo adachotsedwa dzuro Lachinayi masana. Matupi 6 omwe apezeka aja atengedwera ku mabanja awo ku Banyuwangi, akuluakulu aboma adatero.

Munali anthu 53
Anthu 30 Ali safe apulumusidwa
Anthu 6 apezeka atafa
Meaning while anthu 17 sanapezeke

Follow Malawi VLOG for more news and entertainment

Your girlfriend looking at you because you're watching Super League matches at a time she is supposed to be watching Zee...
28/06/2025

Your girlfriend looking at you because you're watching Super League matches at a time she is supposed to be watching ZeeWorld movies.

Good morning Neba 🤣

Wokagula  soda 😂
22/06/2025

Wokagula soda 😂

Ife tinakula life ija yoti pa den pakakhala masamba 'atea kulibe,  mastern amatenga sugar ndikumuika pa spoon ndikuotcha...
22/06/2025

Ife tinakula life ija yoti pa den pakakhala masamba 'atea kulibe, mastern amatenga sugar ndikumuika pa spoon ndikuotcha pa Moto, Zimakhala zatheka

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi VLOG posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi VLOG:

Share