De Gist

De Gist Latest gossip, breaking news and stories

28/07/2026

Rudoh Kodi apepesee?

27/07/2026

If Wahala was a person

Mapangizo kwa Abwenzi:Abwenzi mukuoneka kuti mumakingoza anthu ndalama kwambiri, which is chinthu chabwino chifukwa muma...
26/07/2026

Mapangizo kwa Abwenzi:
Abwenzi mukuoneka kuti mumakingoza anthu ndalama kwambiri, which is chinthu chabwino chifukwa mumafuna kuthandiza.

Vuto lanu Abwenzi ndi lakuti, muli very naive, too trusting kwambiri. Kapenatu umphawi mumaumvetsetsa kuposa umphawiwo.

Ku kongoza munthu sumupatsa popanda signed agreement, olo muli ndi ID ya Tendai sizokwanula, akhinzanso kunena kuti munamubela ID. Mumafunika anthu awiri ma witness ku siyinira kuti mukukongoza munthu ndalama. Apapa ka kwana kachiwiri mukubwera ndi ya ngongole. Tapangani jack up it's 2026. Adzipita Ku bank or akatenge payday loan.

26/07/2026

No no no!!🤣🤣🤣

25/07/2026

A Ex zikuvuta

25/07/2026

Za ma luv... A bambo Shonga, page yawo yanyuwani nyimbo yoyamba kuphulitsa kawawa, ndeu ndeu ndi mkazi wamwini💥🔥

👑 Miss Malawi Bombshell bomb 💣💥: New Statement Reveals Why Thandie Didn't Go to Miss Universe.  Aubrey Kusakala, Directo...
24/07/2026

👑 Miss Malawi Bombshell bomb 💣💥: New Statement Reveals Why Thandie Didn't Go to Miss Universe.

Aubrey Kusakala, Director of Communications for Prophet Shepherd Bushiri and Goshen Citysays that reigning Miss Malawi Thandie Chisi was offered the opportunity to represent Malawi at Miss Universe but declined for personal reasons.

When another international pageant opportunity became available, the Miss Malawi Secretariat selected first runner-up Ireen Navicha in line with the organization's policy of allowing runners-up to take international opportunities if the winner is unavailable.

It also clarifies that Goshen City is only the pageant's sponsor, not its administrator, so decisions about contestants are made by the Miss Malawi Secretariat and Board. While acknowledging communication and contractual issues, the statement urges the public not to blame the sponsors for decisions outside their control and calls for unity, fairness, and putting Malawi's interests ahead of personal disputes.

24/07/2026

De Gist.. Emmie walangiza my gender, kumaupeza mtima.

Address

Barking

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when De Gist posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share