
30/07/2025
Ulendo okapereka zikalata ku ofesi ya MEC kwa yemwe akuyimira ku Mulanje Pasani Constituency ngati phungu wachipani cha DPP ku nyumba ya malamulo Hon. Ebbie Mathanda uli mkati padakali pano ndipo akasiya makalatawa pa Chambe TDC.
zikalatazi ndizowalola mayi Ebbie Mathanda kuti azathe kupikisana nawo pa zisankho zomwe zichitike pa 16 September, 2025.