07/08/2025
Have Haye
Lelo tigawaneko chimodzi chonkha.๐โโ๏ธโน๏ธ๐
Ndili ku form 1 ndi nkaphunzila day secondary๐ฏ,
Amayi anga anali a nurse,komano akapeza nthawi amaphika zogulitsa,ngati ma sikono,mandazi.๐๐ค
Ndisanapite sukulu ndimatenga kukagulitsa.sukulu ๐บ
Amayi anga amandilandila ndikabwelako,amakagulitsa ku chipatala kwa anthu akusikelo,ma staff.๐จโ๐ป๐งโ๐จ
Ifenso timakagula pa buleki.๐ช๐๐ฐ๐งโ๏ธ
Ndiye mandasi anandiphunzitsa kupanga bizimesi. ๐คท
Ndinaphunzila kulawilila popanga zinthu.๐ฆพ๐ช
Uthenga wanga upite kwa achinyamata omwe tikanasungidwa makomo mwa makolo anthu.๐จโ๐ฉโ๐งโ๐ฆ๐จโ๐ฉโ๐ฆ
Kaya ndiwe mwana wapakhomopo wobelekedwa,kaya wa chibale,kaya oleledwa chabe.๐จโ๐ฉโ๐งโ๐ฆ๐จโ๐จ
Kumathandiza makolo anu.๐โโ๏ธ๐
Nthawi zina sudziwa kuti mandazi akuphika akukuphunzitsa bizimesi ina yake.๐
Mukayamba kukhala panonkha mudzidzakumbikila kuti kwanthu timatele.๐ญ๐คฝโโ๏ธ๐ต
Phunzilani ntchito zapakhomo.๐จโ๐ฉโ๐ฆ๐จโ๐ฉโ๐งโ๐ฆ
Osati koma ndiye kwathu amandizuza,ngati akuzuzani ndipo pali umboni ,pitani kumalo oti akhoza kukuthandizani mukadandawule.๐ฎโโ๏ธ๐ฎโโ๏ธ
Mandazi anga amatha nsanga chifukwa azanga onse amandigula,komaso ndikavalilatu uniform amati timugule ameneyu azipa ku sukulu .๐งโ๐ป๐ฉโ๐ป