Zikomo Social Net

Zikomo Social Net Where words spark Change!! Entertainment hub .For promotions and extra call on 0884 88 2794/991440060
(2)

21/09/2025

Omanu akufuna agone muli ndi Mawu?
Komah Baddie eeeshi

21/09/2025

Ukakhala Single Munthu thawi yayitali Mutu wako sumagwira bwino bwino ntchito 😊

21/09/2025

Kuwononga mbiri yabwino, ndikophweka,😂😂😂😂

Koma kuti uyikonzeso mmmm sizophweka 🤦🤦🤦🤦🤦🤦

21/09/2025

Chimene umafuna nzako atakuchitira, uyambe iweyo kuchitira ena | chimene sungakondwe nzako atakuchitira, iweyo usachitire wina |

Full Time Manchester City (1)-(1) Arsenal
21/09/2025

Full Time
Manchester City (1)-(1) Arsenal

21/09/2025
21/09/2025

Yabweza Arsenal

21/09/2025

Sikachibwezi kaja madalira kapita Ku School 🎒..Apapa tafananatu tiyambe kucheza

21/09/2025

Mmmh Amatikondadi zeni zeni Makolo Anthu omwewa.

21/09/2025

Half Time
Arsenal 0 Vs 1 Manchester City

21/09/2025

Game ndi 90 Minutes

21/09/2025

Arsenal 0- 1 Manchester City

Address

Nairobi

Telephone

+265991440060

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zikomo Social Net posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Featured

Share