Balaka Shire North News Update

Balaka Shire North News Update News that are carentry in shire north and world..

07/01/2025

Doctor kondwani nakhumwa alonjeza zozatenga boma pa zinsakho zomwe zichitika museptember

07/01/2025

Odziwa zanyengo ati vula ikhala ikuvuta pali chiopsyezo chokuti madzi atha kusefukila

25/10/2024

Anzanyengo alangiza anthu omwe amama mowa mwauchidakwa kuti achepese malomwake ayambe kumwa madzi pafupipafupi kambakoti dzuwa likulakwambili Mandela amangochi ndi mphepete mwa shire

09/10/2024

Apolice atsimikiza za imfa ya bambo wina kushire kamba koti wagwidwa ndi ng'ona am'bupha ati bamboyi amachokela kumphimbi.

08/10/2024

Welcome To Balaka Shire North News Updateโœ‹โœ‹๐Ÿ‘๐Ÿ‘€

08/10/2024

Nagti ulinawo moyo is gift from God

Address

Shire North
Balaka

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Balaka Shire North News Update posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share