Bangwe Tv

Bangwe Tv Bangwe Tv is an online Television channel dedicated to promote Bangwe Content to masses of people worldwide.

07/06/2026
Ife a Bangwe TV ndi okhuzidwa ndi imfa ya Bambo Lester omwe anali mmodzi mwa ma drivers a Hon Orphan Shaba. Bambo Lester...
07/06/2026

Ife a Bangwe TV ndi okhuzidwa ndi imfa ya Bambo Lester omwe anali mmodzi mwa ma drivers a Hon Orphan Shaba. Bambo Lester anagwira nafeso ntchito nthawi ya Bangwe Got Talent potithandiza kunyamula zina ndi zina zofunikira. Mzimu wawo uwutse mu mtendere 😭

Ngati zabo koma ayi zikuchitikadi ndithu, kuyambira lero azitchulidwa kuti Zonke Madness
06/06/2026

Ngati zabo koma ayi zikuchitikadi ndithu, kuyambira lero azitchulidwa kuti Zonke Madness

06/06/2026

Budding female musician from Bangwe Nthandizi, Memory Mhone aka Emm Star continues to raise her music profile with the release of a new single "Tili Cho" today.

The youthful musician who idolises Tuno and Zuchu described the song as a party anthem which celebrates good life.

It's music video shot and directed by VJ Ropczo is accessible on
https://youtu.be/Ln9-8SG-eaE?si=Z7pXoh6U5_eYjLkq

Olo mbiri ya chibwezi alibe, Happy Birthday DJ Khoo wakwa Namoyo
06/06/2026

Olo mbiri ya chibwezi alibe, Happy Birthday DJ Khoo wakwa Namoyo

05/06/2026



Heavy police presence currently being observed in Bangwe. Pomwe anthu ena akunena kuti awona aPolice akuwomba mfuti kangapo pamalo ena omwela mowa pa chikunda kenako awona ma galimoto aPolice ochuluka akuzungulila ku Bangwe.

Happy Birthday photographer mwayie snooker ambiri akuti sanayambe amuwonapo atavuta chipewa
02/06/2026

Happy Birthday photographer mwayie snooker ambiri akuti sanayambe amuwonapo atavuta chipewa

01/06/2026

Happy Birthday to Businessman Israel Chinsinga aka Bangwe Tycoon. 🎂🎂.

With heavy hearts, we announce the passing of Mwayi Kabuthu. Our thoughts and prayers are with his family and loved ones...
30/05/2026

With heavy hearts, we announce the passing of Mwayi Kabuthu. Our thoughts and prayers are with his family and loved ones during this difficult time.

🕊️ Rest in Peace, Mwayi.

30/05/2026

Ma Gunners aku Ghana eeeeeee 🙌🙌

Address

Bangwe
Bangwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bangwe Tv posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category