ToniCity 265

ToniCity 265 Your Favourite Beat Plug
(1)

Ndakwatira lero 🤣🤣jokes congrats Ufulu
11/10/2025

Ndakwatira lero 🤣🤣jokes congrats Ufulu

09/10/2025

🔥NEW FREE BEAT ALERT🔥
Dropping 11, Link in the comment section

Send a message to learn more

08/10/2025

New song on the way

08/10/2025

When should I drop this one? Ndithandizeni date

07/10/2025

Ka moyo kosampula Ndi kuba ma beat pa YouTube ka ka kuchulukira one day tizapeza nyimbo zambiri zotchuka kumalawi kuno azithothola from streaming platforms because 90% of the music out here ma beats ake Ndi osampula kapena kugwiritsidwa opanda chilolezo.

How hard is it to find a producer and create something from scratch? Kusafuna kulipira kapena Kusafuna kutukulana?

06/10/2025

Tidrope aka? Featuring x x

05/10/2025

Studio is open today, book your sessions

04/10/2025

Let's make hits today, studio is open

02/10/2025

As they say "an early bird catches the worm"

Studio is open today book your sessions now 🔥

Za economy yathu tonse tikudziwa, ife titaona kuchulukira kwa anthu odandaula zachuma tati tikuthandizeni chonchi. Muzip...
30/09/2025

Za economy yathu tonse tikudziwa, ife titaona kuchulukira kwa anthu odandaula zachuma tati tikuthandizeni chonchi. Muzipeleka subscription ndithu nyimbo zomwe mungapange record zizitengela ndi chAngu chanu pa mic. Do you think it is a good idea? Zikomo

19/09/2025

Filani ndipo simukhumudwa

🎤 ArtRosetta
Malawian Rapper • Dancer • Performer
📍 Blantyre, Malawi
🔥 Serving bars & moves that inspire the culture
📲 Management: +265 881 12 61 27

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ToniCity 265 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to ToniCity 265:

Share

Category