LWC Radio

LWC Radio LWC Radio 96.0 FM Southern region 96.2 FM Central region. Http://livingwaters-dexterity.radioca.st/stream

 Sadzi Community Day Secondary School Waste Management Club in partnership with Zomba Waste Advisor have ventured into a...
16/10/2025



Sadzi Community Day Secondary School Waste Management Club in partnership with Zomba Waste Advisor have ventured into a program of turning waste products into fertilizer and other items such as doormats and moppers among others.

Chairperson for Zomba Waste management Thandie Kaufulu Kasiyamphanje, highlighted that what's so special with the fertilizer is that it is produced using the resources which are locally available.

On his part, Chairperson of the club Paul Knix expressed optimistic that the production of such type of fertilizers with high quality will still sustain the program of helping the needy students at the school.

Meanwhile, the school's Club Secretary, Vannesa Blazzio, a form 3 student at the school said that students are delighted at the initiative benefits both the students as well as the community at large.

Reported by Clifford Kalilombe Jr, (Zomba)

15/10/2025

Madzulo uno pa LWC Radio, nthawi ya 7 koloko tikhala tikukupasirani program yapadera ya Anakubala Special.

Mverani komanso kutsatira wayilesi imeneyi pa 92.0 chigawo chakummwera komanso 92.2 chigawo chapakati.

 Yemwe anali Prime Minister m'dziko la Kenya, Raila Odinga wamwalira. Odinga wamwalira ali ndi za 80.Malipoti otsimikizi...
15/10/2025



Yemwe anali Prime Minister m'dziko la Kenya, Raila Odinga wamwalira.

Odinga wamwalira ali ndi za 80.

Malipoti otsimikizika akuti Odinga wamwalira akulandira thandizo la mankhwala ku India.

Malinga ndi achipatala, Laira Odinga wamwalira chifukwa cha mtenda ya mtima (heart attack).

Raila Odinga anabadwa mu 1945 ndipo anakhala Nduna yaikulu ya Kenya kuyambira chaka cha 2008 mpaka 2013.

Anali m'modzi mwa atsogoleri odziwika kwambiri ku Kenya komanso wotsutsa boma kwa nthawi yaitali.

From LWC radio to All Mothers
15/10/2025

From LWC radio to All Mothers

15/10/2025

Lero ndipa 15 October 2025, tsiku lokumbukira anakubala. Anyadireni amayi anu powatchula dzina komanso kutchula langizo limodzi lomwe mumalikumbukira.

LWC Radio 96.0 and 96.2

 Ayiya company, the organisers of Praise Experience Malawi said they want to bridge the gap that is there between vetera...
10/10/2025



Ayiya company, the organisers of Praise Experience Malawi said they want to bridge the gap that is there between veteran gospel artists and upcoming gospel artists.

Poyankhula ndi olemba nkhani muzinda wa Blantyre, mkulu wa bungweli a Jones Mbela ati abweretsa pamodzi oyimbawa ndi cholinga chofuna kufikira anthu ochuluka ndi nyimbo zauzimu kuchokera kwa oyimba nyimbo zauzimu.

A Mbela anaoitiliza kunene kuti akuyembekezera oyimba osachepera 30 pamwambo wawo omwe uchitikre pa 29 November chaka chino Ku holo ya COMESA muzinda wa Blantyre.

'Pa oyimba 30 amene azaimbe pa mwambo wakuno Ku Blantyre, aliponso ena 30 omwe ndiokonzeka kuti akaimbenso Ku Lilongwe', atero a Mbela.

My mau make modzi mwa oyimba nyimbo zauzimu Dr Ethel Kamwendo Banda wati uwu ndi mwayi waukulu omwe anthu okonda nyimbo zauzimu alinawo Ku Blantyre potengera kuti oyimba okwana 30 kubwera pamodzi sizophweka koma zatengera kampani ya Ayiya kuti izi zitheke.

Ena mwa oyimba omwe akaimbe pamwambo waku Blantyre ndi monga Ndirande Anglican voices, Dr Ethel Kamwendo Banda, Favored Martha, Isaac Chizaka, Maggie Mangani, Phallyse Mang'anda mwa ena.

Wolemba Mphatso Nkhoma (Blantyre)

 Mneneri wa mtsogoleri wa dziko lino, a Shadric Namalomba, wati amva kupepesa komwe mkulu wa kanema wa MBC, a George Kas...
10/10/2025



Mneneri wa mtsogoleri wa dziko lino, a Shadric Namalomba, wati amva kupepesa komwe mkulu wa kanema wa MBC, a George Kasakula, wapereka kwa a Peter Mutharika. Komabe, a Namalomba ati chipani cha DPP chidzadikirira kaye yankho la mtsogoleri wa chipanichi, a Mutharika, kuti awone ngati alandira kupepesako.

Polankhula ngati mneneri wa chipani cha DPP, a Namalomba ati sakudabwa ndi kupepesa kwa a Kasakula chifukwa akudziwa bwino kuti a Mutharika anachitiridwa chipongwe chachikulu pa MBC.

"A Mutharika akhala akulemba makalata ku MBC, ku MACRA, komanso ku MISA Malawi, akupempha kuti MBC makamaka a Kasakula asiye kuwanyoza, Koma zonse zinali ngati kulankhula ndi khoma ndipo a Mutharika adandaulapo pa misonkhano, akuchonderera kuti zomwe a Kasakula amapanga si zabwino, koma sanamvele madandaulo awo," atero a Namalomba.

A Namalomba ati kupepesa komwe kwachitika lero kwaonetseratu kuti a Kasakula akuvomereza kuti anachita zolakwa.

Iwo akupempha komiti ya chilango ya MBC kuti iunikire bwino momwe ntchito zinagwiridwira.

Lero, a Kasakula apepesa a Mutharika pa zonse zomwe ankawanena pa MBC m’nthawi ya kampeni. Kupepesaku kwachitika pa kanema wa MBC.

Wolemba Abdullaziz Losa

 Mpingo wa Church of Central Africa Presbyterian (CCAP) pansi pa Nkhoma Synod wasankha atsogoleri atsopano pa msonkhano ...
10/10/2025


Mpingo wa Church of Central Africa Presbyterian (CCAP) pansi pa Nkhoma Synod wasankha atsogoleri atsopano pa msonkhano wawo wa 41st Biennial Conference womwe wachitika posachedwapa.

Pa msonkhanowu, maudindo osiyanasiyana asinthidwa ndipo anthu otsatirawa asankhidwa kuti azitumikira mu maudindo awa:

- Synod Moderator: Rev. Nyasulu
- Vice Moderator: Rev. Yasin Gama
- Synod Clerk: Rev. Kuthyola Mwale
- Deputy Synod Clerk: Rev. Tamale
- Synod Actuarius: Rev. Jere
- Executive Member: Elder Lot Dzonzi
- Executive Member: Elder Chulu
- General Secretary: Rev. Brian Kamwendo
- Deputy General Secretary: Rev. J. Kachipanda

Kusankhidwa kwa atsogoleri atsopanowa kukuyimira gawo lofunikira pa ntchito ya mpingo, pomwe akuyembekezeka kutsogolera ntchito za mpingo ndi kulimbikitsa chikhulupiriro m’madera osiyanasiyana a Nkhoma Synod.

Wolemba : Abdullahziz Losa

Big shout out to our newest top fans! 💎 Aubrey Vincent Lonex, Beck Namo, Kenedy Palana Favour, Grace Nsaku, Stella Kutin...
09/10/2025

Big shout out to our newest top fans! 💎 Aubrey Vincent Lonex, Beck Namo, Kenedy Palana Favour, Grace Nsaku, Stella Kutinyu, Christopher Khoromana, Henry Kachigwada, Bleśsed Elisah MW, Ted Likombola, Chifuniro King Mavwere, Thokozire Zalira

Drop a comment to welcome them to our community,

 The newly recruited Teachers under IPTE 14-17 Cohorts in Blantyre Urban are demanding answers for their unpaid salaries...
09/10/2025



The newly recruited Teachers under IPTE 14-17 Cohorts in Blantyre Urban are demanding answers for their unpaid salaries for the month of September this year.

The teachers are currently gathered at Blantyre Urban DEM offices where they want answers from the authorities on their petition.

They attribute that most of the councils, received their September perks and it is only them who are yet to get theirs and as well no communication was made to them for the delays.

Reported by Mphatso Nkhoma (Blantyre)

  Ntchito yowerengela mavoti yafika kumapeto muzinda wa Blantyre.Mu Blantyre district council mudali madera aphungu okwa...
19/09/2025




Ntchito yowerengela mavoti yafika kumapeto muzinda wa Blantyre.

Mu Blantyre district council mudali madera aphungu okwana asanu ndi limodzi(6).

Ndipo umu ndimene zotsatira zosatsimikizika zilili.

Peter Muthalika DPP 118,691
Dalitso Kabambe UTM
5,158
Lazerus Chakwera MCP
5,002
Atupele Muluzi UDF
3,568
Joyce Banda PP
687
Mphuziro Mvula Independent
277
Chibambo kamuzu independet
236
Bandawe akwame AAA
262
Banda Thokozani
297
Chilungo Adil James independent
137
Chipojola Cosmas Felix independent
136
Mwenefumbo FrankTumpale
56
Sauti Jordan P*P
53
Swira Smart Mulumbe independent
29
Miwald Tobias
23
Kondwani Nankhumwa PDP
89
Michael usi Odya zake
279

Wolemba Moses Byson (Blantyre)

Address

Blantyre

Telephone

+265999878093

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when LWC Radio posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to LWC Radio:

Share

Category