IB Entertainment

IB Entertainment photographer
(1)

SINDI  upcoming wa Ken B Wazakena Ken B Wazakena  wati iye ndi upcoming oyamba kufikila 40k in 24 hoursNyimbo in the com...
09/07/2025

SINDI upcoming wa Ken B Wazakena Ken B Wazakena wati iye ndi upcoming oyamba kufikila 40k in 24 hours
Nyimbo in the comment section 👇

NJIRA ZOPHERA MWAMUNA UKATOPA NAYE```Mzimai wina atatopa nalo banja lake anafuna kungopha mwamuna wake ndipo anapita kwa...
07/06/2025

NJIRA ZOPHERA MWAMUNA UKATOPA NAYE

```Mzimai wina atatopa nalo banja lake anafuna kungopha mwamuna wake ndipo anapita kwa amayi ake kukafunsa njira imene angamuphere mwamuna wina aliyense popanda wina aliyense kuziwa kuti wachita izi ndi iye.
Ndipo atauuza amai ake anam***andiza motere, mzotheka mwana wanga zomwe ukufunazo koma, ziwa ukuenela kupanga kaye zinthu zoti anthu asakhulupilire kapena kuganiza kuti wachita ndi iwe, nde ukuenela kuchita izi

_💠 Uzimukonda kwambiri mwamuna wako, kuposa wina aliyense.

_💠Usapange zinthu zoti m***a kuyambana nyumbamo kwa miyezi itatu.

_💠 Uzimuchitila nsanje kwambiri.

_💠 Akakupasa ndalama osamanyinyi ngakhale ili yochepa.

_💠 Uzimulemekeza kwambiri.

_💠Usapange zinthu zomuphyesa mtima.

_💠 munthawi ina iliyonse mupase mwachikondi.

_💠Mukamakangana chonde osamakweza mau, ndipo iwe kwako kuzikhala kupepesa basi kuopa kuti anthu angakumvereni kuti mukukangana.

_💠Uzionesesa kuti mtendere ndiumene ukumanga nthenje nyumba mwako.

Ndipo mai anafunsa ukwanisa? mzima anayankha eya ama, ndipo anampasa tiufa ndipo anati uyu ndi tamerc ndipo uzithira muchakudya cha mwamuna wako daily kwa masiku makumi atatu.

Patangodusa makumi atatu mzimai uja anapitaso kwa amayi ndipo anati ama, mwamuna wanga uja wasinthiratu sindikufunanso kumupha chonde pangani zoti tarmec uja asagwirenso ntchito chonde ama, ndikamupha sindizapezanso mwamuna wabwino ngati amene uja.

Ndipo amai aja anaseka, ndipo anati:

kkkkkkk kuterokotu ufa uja sanali tarmec ayi, unali ufa chabe
chimene chimasowekela mwa iwe anali malangizo amene ndinakupasa aja, waona? Mwamunayotu sanasinthe ayi ndi yemwe uja... koma iwe ukumuona kusintha chifukwa iwe mwini wasintha chikhalidwe, mwana wanga banja ndi chikhalidwe, chikhalidwe mchomwe chimapangisa kuti banja likhale lokoma.

Kuyambira lero uzisatila malangizo amene ndakupasa kuti banja likhale lolongosoka```

Let’s show lov to Waxy kay by sending him birthday wishes msgsAnd lyk this photoTayambapo(Happy birthday to u Waxy Kay)
04/06/2025

Let’s show lov to Waxy kay by sending him birthday wishes msgs
And lyk this photo
Tayambapo(Happy birthday to u Waxy Kay)

30/05/2025

Mmalawi simunthu wamba,mwaimva kale iyi???

World Boss tour 2025    Follow IB Entertainment
28/05/2025

World Boss tour 2025
Follow IB Entertainment

Kodi iyi mudaonela kale Tiyeni  ku YouTube channel yathu tikaonele komaso tipange subscribe
27/05/2025

Kodi iyi mudaonela kale
Tiyeni ku YouTube channel yathu tikaonele komaso tipange subscribe

IB Entertainment had a chance to know the story behind Zeze Kingston music.

26/05/2025

Kukakozeka basi

Food competition Spanner 🇲🇼 Malawi vs AlexAlex walonjeza kuti akangoluza amugulila Spanner plot Tione madzulo ano kuti a...
24/05/2025

Food competition Spanner 🇲🇼 Malawi vs Alex
Alex walonjeza kuti akangoluza amugulila Spanner plot
Tione madzulo ano kuti atapambane ndani
Awali Austin

23/05/2025

Zinalikotu ku Chirimba ku

23/05/2025

IB Entertainment inali mu Chirimba mu gululu ndi izi

CONFIRMED Scorchers ikumana ndi team ya Morocco  pa bingu national stadium pamasewera opimana mphamvu , ndipo coach Love...
23/05/2025

CONFIRMED

Scorchers ikumana ndi team ya Morocco pa bingu national stadium pamasewera opimana mphamvu , ndipo coach Lovemore fazili akhale akulengeza m'ndandanda wa osewera tsiku linalililose.
Big up Scochers

Kumawelenga ma buku kumeneko🤣🤣🤣
22/05/2025

Kumawelenga ma buku kumeneko🤣🤣🤣

Address

Blantyre

Telephone

+265993501123

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when IB Entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share