Pamudzi TV

Pamudzi TV Arts & Entertainment

17/08/2026

Koma ichi chimatha kuichemelera eee

17/08/2026

Shaa mwana uja wasatira aphunzitsi ake kunyumba kwawo

17/08/2026

Umunthu uja ndi ofunika banja limafuna umunthu osati mawonekedwe

17/08/2026

Ku school kuja kumachitika zinthu anawa amakumana ndizambiri

16/08/2026

Atakanidwa chibwenzi ndi mwana wa school basitu anangoyamba zojama yake mu class

16/08/2026

Inu mukanatani mene zililimu?

16/08/2026

Koma mpaka mwana kumuyankhulira ma script a shakespeare? Atsikana muphunzire kukana ngati Bella yu

15/08/2026

Sionse koma pali ena mwa aziphunzitsi amafuna azikhala pa ubwenzi ndi ana a school... Izi zimasokoneza anawa

15/08/2026

Anatengeka ndi mzake waku town chifukwa chotchena lero watenga nazo mimba

15/08/2026

Ubwenzi wake ndi achidya makanda unayambira pomwe ankafuna thandizo lakuchipatala.... Koma sanasiyire pompo mpaka anamupatsira matenda, atsikana pewani makhalidwe ngati awa

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pamudzi TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share