
26/09/2025
MTENGO WA CHIMANGA WASIKA KUCHOKA PA K78 000 KUFIKA PA K45 000 THUMBA LA 50KG MUMADELA AMBILI ADZIKO LINO
Mtengo wa chimanga sopano wasika kuchoka pa K78 000 kufika pa K45 000 thumba la 50kg.
Pali chiyembekezo choti chimangachi chitha kusika mpaka pa, K20 000 thumba pa K50kg kaamba kakusankhidwa kwa a, Professor Arthur Peter Muntharika.
Nayo dollar yaku America yagwa mphavu pa black market kuchoka pa K5 000 kufika pa K2500.
Tiyembekezele kusikaso kwazakudya ndi katundu mumasiku ochepa omwe akuzawa.