Heavenly NewsHub-INTEL

Heavenly NewsHub-INTEL End Times Christ News and Current Affairs Reliable Breaking News Source, and Anti Fakenews Media Gr

ANYAMATA A ILLUMINATI KU MALAWI AYAMBA KUDZIULULA POYERA - NTHAWI NAWO YAWATHERA SANGAZIBISENSO.PAMENE OYIMBA ANGAPO AKH...
14/10/2023

ANYAMATA A ILLUMINATI KU MALAWI AYAMBA KUDZIULULA POYERA - NTHAWI NAWO YAWATHERA SANGAZIBISENSO.

PAMENE OYIMBA ANGAPO AKHALA AKUMWALIRA MU INFA ZOSAMVETSETSEKA MOTSOGOZANA MCHAKACHI, NKHALAKALE PA ZOIMBAIMBA YEMWE ALI NDI ZIZINDIKIRO ZONSE ZA ILLUMINATI WATULUTSA NYIMBO YOTCHEDWA INFA. AKUTITU NGATI SAKUDZIWA CHENICHENI CHIMENE CHIKUCHITIKA PA INFA ZA ANZAOZI.

PODZIULULA YEKHA MKHALAKALEYU, CHOMWE CHIKUONEKERATU KUTI NDI SATANIC RITUAL KWA ANTHU OZINDIKIRA, WAJAMBULA KANEMA YA NYIMBOYI IYE ATAGONA M'BOKOSI LA MALIRO.

MWA ZINA, IYE POPANGA PROMOTE NYIMBO YAKEYI WAJAMBULITSA CHITHUNZI NDI A COLLINS MAAGALASI ONSE MU UWIRIWAWO ATAPANGA CHIZINDIKIRO CHA ANTHU A KU CHIPEMBEDZO CHA SATANA POPEREKA ULEMU KWA MULUNGU WAO SATANA - DEVIL'S HORNS SIGN (CHIZINDIKIRO CHA MINYANGA YA SATANA).

A COLLINS MAGALASI MZAKE WA PONGA APA NANE NDIPONDEPO WA A DOROTHY SHONGA WAGULA NYIMBO IMODZI YOPANDA TANTHAUZOYI PA MTENGO WA K3.5 MILLION KWACHA. PAJA KU CHIPEMBEDZO CHA SATANA NDALAMA NGATI AMATI NDI MA PINATSI (PEA NUTS) KOMA KWA MUNTHU OGWIRA NTCHITO MU CHOONADI NDI NDALAMA YA MBIRI.

A COLLINS MAGALASI NDI A DOROTHY SHONGA ADAPEZEDWA NDI MLANDU OTI AYANKHE NDI KHOTHI.

A MAGALASI ADALI BWANA WA NKULU KU MALAWI ENERGY REGULATORY AUTHORITY (MERA) NDIPO IWO AKUIMBIDWA MLANDU WA KUTI IWO NDI DOROTHY SHONGA MU UWIRIWAWO ADATSEGULA KAMPANI. IWO POGWIRITSA NTCHITO MPHAMVU ZA UDINDO WAWO KU MERA ADAPELEKA MWAI WA BUSINESS KANGAPO KUCHOKA KU MERA KUPITA KU KAMPANI YEMWE MWINI WAKE NDI DOROTHY SHONGA NDI IWO ENI.

MA BUSINESS AMENE KAMPANI YA ANTHU AWIRIWA IDACHITA NDI MERA MOSATSATA NDONDOMEKO NDALAMA ZAKE ZIKUPOSERA K186 MILLION KWACHA (186 MILLION PEANUTS MONGA MOMWE AINIAKE AMAYENERA)

THAWANI NYIMBO KOMANSO ANTHU MACHITACHITA OTEREWA.

AMENE MUNATEMBELEREDWA KUKONDA NYIMBO ZA ANTHU OTEREWA, BOKOSI LA MALIRO LIMENELI LIKUSAKASAKA MUNTHU MNYUMBA MWANU, MBANJA MWANU KAPENA ABALE OKONDEDWA KU MUDZI KUTI APITE KULI CHETE MWADZIDZI.

1 Thessalonians 5:22.
22. Flee from every appearance of evil.
[22. Mupewe maonekedwe onse a choipa.]

GALAMUKANI A MALAWI, TSEGULANI MASO.

Heavenly NewsHub-INTEL
DEVINE INTEL

14/10/2023

KANEMA YA PASTOR BENNY HINN YOLAPA NDI KUSINTHA UTUMIKI WAO PA ZA UTHENGA WA ZOKONDWERETSA ZA MDZIKO NDI THUPI (PROSPERITY GOSPEL AND FEEL GOOD MESSAGES )

MUNDIKHULUKIRE KAMBA KA UTHENGA WANGA WA ZOKONDWERETSA ZA MDZIKO NDI KULEMERA OMWE NDAKHALA NDI KUPHUNZITSA MU ZAKAZI - MBUSA BENNY HINN

IYE WATI SAKUFUNA KUDZAKANIDWA KAPENA KUDZAIMBIDWA MLANDU PA TSIKU LOMALIZA KUMWAMBA UKATHA MOYO UNO

MBUSAYU WATI NCHOLAKWIKA KUIKA MTENGO (KU TCHAJA) NDALAMA PA UTHENGA WA MULUNGU NDI MAPEMPHERO A ZOZWIZA ZOCHOKERA KWA MULUNGU.

A BENNY HIN WATI ALI OKONZEKA KU LUZA ABALE OMWE SAMULANDIRA NDI KAYENDEDWE KATSOPANOKA MU UTUMIKI WAKE

Heavenly NewsHub-INTEL to James Phiri
________________________________________________________

"FORGIVE ME FOR MY TEACHINGS OVER THE YEARS ON PROSPERITY! Pastor Benny Hinn.

A well known Israeli Christian Televangelist, Pastor Benny Hinn in a video an hour ago on Facebook has apologized to his members over his false teachings on prosperity, sowing of seed and monetizing the gospel.

According to the pastor while pleading with the entire Christian body to forgive him, he doesn't want to be rejected in Heaven on the last day. He also went further to say that he wanted to say this long ago but be couldn't.

According to Pastor Benny Hinn from the video: "The flesh must be out of the way for men to make it to Heaven on the last day. Teaching on prosperity is a feel good message. I am sorry to say this that prosperity has gone a little beat crazier this time around and today, I want to correct my own theology about prosperity gospels, sowing of seeds and monetization of the gospel. When I read the Bible now, I don't see it with the same eye I saw it 20 years ago.

"The Magazine will normally publish was from my father-in-law. I inherited it because I married his daughter. It was a channel for monetizing the Gospel. It is an offense to the Holy Spirit when we receive money on those materials. The gospel is totally free. I am done with anything prosperity gospel and monetization of the gospels.

"This is the first time in my life that I am saying this and I don't care what people think about me anymore. I know many will not invite me anymore and I don't care. I don't want to be rejected on the last day. ndepotv. If you are not giving because you love Jesus, don't bother giving. Giving is making me sick to my stomach and I am free from it now, I don't want to hear anything about sowing of seed anymore.

"I am truly sorry for all these years of false teachings. Please forgive me and do away with my messages on prosperity and sowing of seed".
............................................

MUNDIKHULUKIRE KAMBA KA UTHENGA WANGA WA ZOKONDWERETSA ZA MDZIKO NDI KULEMERA OMWE NDAKHALA NDI KUPHUNZITSA MU ZAKAZI - ...
13/10/2023

MUNDIKHULUKIRE KAMBA KA UTHENGA WANGA WA ZOKONDWERETSA ZA MDZIKO NDI KULEMERA OMWE NDAKHALA NDI KUPHUNZITSA MU ZAKAZI - MBUSA BENNY HINN

IYE WATI SAKUFUNA KUDZAKANIDWA PA TSIKU LOMALIZA

MBUSAYU WATI NCHOLAKWIKA KUIKA (KU TCHAJA) NDALAMA PA UTHENGA WA MULUNGU NDI MAPEMPHERO.

A BENNY HIN WATI ALI OKONZEKA KU LUZA ABALE OMWE SAMULANDIRA NDI KAYENDEDWE KATSOPANOKA MU UTUMIKI WAKE

________________________________________________________

"FORGIVE ME FOR MY TEACHINGS OVER THE YEARS ON PROSPERITY! Pastor Benny Hinn.

A well known Israeli Christian Televangelist, Pastor Benny Hinn in a video an hour ago on Facebook has apologized to his members over his false teachings on prosperity, sowing of seed and monetizing the gospel.

According to the pastor while pleading with the entire Christian body to forgive him, he doesn't want to be rejected in Heaven on the last day. He also went further to say that he wanted to say this long ago but be couldn't.

According to Pastor Benny Hinn from the video: "The flesh must be out of the way for men to make it to Heaven on the last day. Teaching on prosperity is a feel good message. I am sorry to say this that prosperity has gone a little beat crazier this time around and today, I want to correct my own theology about prosperity gospels, sowing of seeds and monetization of the gospel. When I read the Bible now, I don't see it with the same eye I saw it 20 years ago.

"The Magazine will normally publish was from my father-in-law. I inherited it because I married his daughter. It was a channel for monetizing the Gospel. It is an offense to the Holy Spirit when we receive money on those materials. The gospel is totally free. I am done with anything prosperity gospel and monetization of the gospels.

"This is the first time in my life that I am saying this and I don't care what people think about me anymore. I know many will not invite me anymore and I don't care. I don't want to be rejected on the last day. ndepotv. If you are not giving because you love Jesus, don't bother giving. Giving is making me sick to my stomach and I am free from it now, I don't want to hear anything about sowing of seed anymore.

"I am truly sorry for all these years of false teachings. Please forgive me and do away with my messages on prosperity and sowing of seed".
............................................

13/10/2023

MBIRI YA MPINGO WA ORTHODOX CATHOLIC CHURCH - ADASIYANA BWANJI NDI ROMAN CATHOLIC CHURCH?

BISHOP YEMWE ANALI WA A KATOLIKA A KU ROMA ADATSUTANA NDI PAPA PA NKHANI YOTI A NSEMBE AZIKWATIRA NDI NKHANI ZINA. PAPA ATATSUTSANA NDI MMAGAINIZO AKE BISHOP WA KATOLIKA WA KU EASTERN EUROPE YU, NDIPO IYE ADAYAMBA KUYENDETSA MPINGOWU NDI MALAMULO AKE, MONGA KULOLA A NSEMBE KUKWATIRA.

PAPA ATAMVA IZI ADAMUCHOTSA MU MPINGO WA A KATOLIKA, NDIPO NAYE BISHOP WA EASTERN EUROPE NAYE ADELENGEZA ZA KUTULUKA KWAKE MU MPINGO WA ROMAN CATHOLIC NDI KULENGEZANSO KUYAMBA KWA MPINGO WA TSOPANO WA CATHOLIC ORTHODOX CHURCH.

NDIPO GULU LOCHULUKA LIDAMUTSATIRA KU MPINGO WAKE WA EASTERN CATHOLIC ORTHODOX CHURCH.

MIPINGO IWIRIYI ZOCHITIKA ZAWO ZAMBIRI NZOFANA PENA NDI PENA.

Heavenly NewsHub-INTEL

Big shout out to our newest top fans this week. Shalom! 💎Leonard Lowole, Gracious Chis, Monica Katentha, Don Bastora, Si...
13/10/2023

Big shout out to our newest top fans this week. Shalom! 💎

Leonard Lowole, Gracious Chis, Monica Katentha, Don Bastora, Simeon Van Rudovic Moyoh, Ibrahim Motani, Chikondi Kalande, Thokozani Frans, Prince Martin, Victor Mthandi, Mungoni Harawa, Esther Luka, Emma Mbewe, Clara Salmon, Chikonzero Wa Devie Rasha, Legina Magodi, Gilbert B Nachongo, Cosmas Msosa, Innocent Khozomba

CHI NJOKA CHIJA CHIDANYENGA ADAM NDI HAVA MMUNDA MUJA CHIKUPITILIZABE KUNYENGEZA ANTHU PA DZIKO LONSE KUTI ASAKAONE NAWO...
13/10/2023

CHI NJOKA CHIJA CHIDANYENGA ADAM NDI HAVA MMUNDA MUJA CHIKUPITILIZABE KUNYENGEZA ANTHU PA DZIKO LONSE KUTI ASAKAONE NAWO MOYO WOSATHA.

KOMA MWA CHISONI WONYENGEZEDWAWO SAKUDZIWA, ONSE ALI MU CHIMTULO CHAKUFANACHO.

DZUKANI!
.........................................................................

CHIVUMBULUTSO 12:9

9. Ndipo chinaponyedwa pansi
CHINJOKA chachikulu, NJOKA YOKALAMBAYO,
iye wotchedwa MDIEREKEZI ndi SATANA,
wonyenga wa DZIKO LONSE; chinaponyedwa
pansi KUDZIKO, ndi angelo ake anaponyedwa
naye pamodzi.

REVELATION 12:9-10 KJV

9 And the great DRAGON was cast out,
that OLD SERPENT, called the Devil, and Satan,
WHICH DECEIVETH the WHOLE WORLD:
he was cast out into the earth, and his angels
were cast out with him.

10 And I heard a loud voice saying in heaven,
Now is come salvation, and strength, and the
kingdom of our God, and the power of his Christ:
for THE ACCUSER OF OUR BRETHREN is cast down,
which accused them before our God day and night.

ON A LIGHTER NOTE..
13/10/2023

ON A LIGHTER NOTE..

13/10/2023

When I was a wizard, I saw one of them. Although I was a witch, I really felt sick when I saw him. I always warn people working in the company because many of you who you call the CEO (Chief Executive Officer) a lot of them are half-demons with half human beings. They are hybrid devils.

Let me talk about what I learned at the magical school in the Kingdom of the Pandemonium.

There are Christians who say that Muslims are our brothers, but they are not. When you call someone a brother, it means you have the same master.

The Bible says that anyone who refuses Jesus Christ is an anti-Christ but Jesus is the way, the truth, the life.

Actually, in the year 630, Lucifer held a meeting in the infernal kingdom with his superior and inferior demons including the infernal princes in order to counter the rising influence of the church.

As a result of that meeting, this Islamic religion came into existence and the Quran was published. This is the antichrist religion orchestrated by the infernal princes and powers of darkness.

Later in the year 715, Lucifer in collaboration with the Roman Catholic church released a powerful and secretive book called Abermale.

But in the year 921 Lucifer himself landed in China and he took human shape and he impregnating a woman. The woman's pregnancy lasted 3 years. The government knew about the pregnancy and they were trying to help her with medication in order to force the delivery.

But it was not working so the woman was put in the hospital and under surveillance. But when the baby was born, he had teeth already and on his head, there were 3 spots. There was a white spot, a red spot, and a black spot. In fact, the baby was even speaking.

After the government saw this, they were afraid. They knew that they were dealing with a paranormal situation and they said to the mother that she cannot keep the child and that the baby must be killed. The government agreed to compensate the mother.

Afterward, the mother then took the baby to the government officials and they threw him in the Hong Kong river in order to kill him.

But a wandering spirit took the baby and transported him to the mountains. They raised him up and fed him until he grew up. He is the man called Lao Tse Tung, the founder of Taoism and he is the initiator of Red Magic.

Actually, the leaders or founders of false religions and sects are demons in the flesh like Lao Tse Tung.

Actually many Congolese musicians and politicians go to China for Red Magic. The movie 36th Chamber of Shaolin was based on Red Magic.

Another movie is called the 7 Secrets of Kung Fu and is also based on Red Magic. Bruce Lee was one of the first modern martial artists to possess these 7 secrets.

That is why even today few can equal his fighting ability and there are Taoism temples everywhere in China.

It is over there that the Congolese musician called Werrason got his kingship and he began to call himself the king of the forest.

This hybrid demon Lao Tse Tung is a dragon, dwelling in the 36th chamber of Shaolin but Bruce Lee managed to enter there and come out alive but few people come out alive.

And our musician Werrason also had been there and he came out alive. In fact, Werrason's album after the visit to China was called Operation Dragon and Bruce Lee's last move was called Enter the Dragon.

I said that the Roman Catholic priest who initiated me in the occult gave me a Satanic calendar containing information about the ruling of times and seasons. The calendar contains the names of demons ruling the days of the week.

Monday is the day Lucifer himself rules on planet Earth and on that day he leaves planet Saturn and his throne and he descends on Earth.

When Lucifer comes down on Earth on Monday from planet Saturn, he comes accompanied with the 24 elders and the 4 living creatures. They come down to earth to cause damages and destruction.

I have a list of many major accidents that happen in our province on Mondays. You remember that 9/11 also happened on a Monday.

And in our country, all the pernicious sects meet on Mondays in the Karavia Hotel to worship the god Lucifer. There are Freemasons, Rosicrucians, Mahikari, and others. Eckankar

I said in the past that Rosicrucian is not a religion or science but a branch of magic and occultism. The devil has managed to intellectualize it and present it to universities as a science but it is witchcraft.

Some people think that white magic is good. Actually, all magics are of the devil. Magic is occultism and Satanism and these are from Lucifer.

Firstly the term magic was used because it was first practiced in the western world and it is practiced mainly by Europeans.

It was when a superior demon called Jesus of London left the planet Saturn and he landed in Europe. He brought this type of magic. This demon is called Belbit by the Romans. He is a superior demon ruling and controlling the European continent.

In White Magic, there are many sects including Rosicrucianism, Freemasonry, Message of Grail, Eckankar.

The giant demon responsible for Eckankar came to earth in the flesh and impregnating a woman and she gave birth to a child called Manta.

Most people in this sect of Eckankar have his photo in their house. This hybrid demon is alive. The initiates of this occultic sect claim that he is the Holy Spirit. This sect is for the intellectual but they used the Bible and they have brochures which are very dangerous.

You can leave your body and go through a wall just by reading their brochures. I said that every Monday the adept of White Magic meet to worship the god Lucifer.

The world leader of Rosicrucianism is called Christian Bernand, a French man. He has a throne. It is established neither in France nor in Paris but in the Slavic realm which is the territory of Rosicrucianism in the realm of Lucifer.

Tuesday is ruled by a demon called Akam. He is called St Francis of Assisi in the popular sectarian church. He has a holiday in his honor, the so-called day of St Francis. He is the demon of division. The devil has assigned him the task of dividing people, even breaking up marriages.

Witches work with him to cause division in the church or in marriages or in families. Many families are divided for a long period of time over things that can be resolved. You see a brother and sister of the same mother and father in grudge forever.

If the devil wants to dislocate a church, he will send Akam. This demon will come to church and impart great knowledge to the members of the church leadership group. As a result, this leader will enter into conflict with his pastor.

And in the end, there will be division and this leader will leave the church with people. They will go to start another church, failing to understand that they are under a curse.

Wednesday is ruled by the goddess Astarte. There are a lot of churches worshipping this goddess. Her name is "Marie de Margue," the so-called Mary, mother of Christ but in reality, the mother of Christ has died a long time ago.

This woman is a demon of space venerated on the 15th of August. She is called by Roman "Mariah Valencia" and she has a baby called Zeus who is the demon of destruction. The baby carried by the so-called Mary in pictures is not Jesus but Zeus.

There is a Congolese musician Papa Wemba who sang for this demon. The name of the son is "Mariah Valencia." The reason Papa Wemba sang for Maria Valencia is that she renewed Papa Wemba's voice and gave him success but in return, he sacrificed babies to her.

In the Arab world, she is called Aicha. There is a musician from Algeria called Cheb Khaled who sang for her and the name of the song is "Aicha I loved you."

In Africa, there is a poem called "African woman." We were reciting it in primary school. Actually, it is a poem in her honor. In Brazil, she is called Makarena.

There is a church that claims that she went to heaven like Jesus on the 15th of August. Actually, on the 15th August, the goddess Astarte came down to earth in a Roman Catholic church and she made a covenant with them.

Before the genocide in Rwanda in 1994, in December 1993, people saw the appearance of this so-called virgin and baby. It was the visit of Ishtar and Zeus. As a consequence, a genocide was orchestrated.

When this goddess and her son Zeus appear in your country, you have to expect bloodshed because Zeus causes tornados, hurricanes, and ecological disasters. This woman is a siren of the world Armstrong. She does not have bones. She is the most beautiful woman in the world.

Lucifer has allocated a whole month for her to be worshipped. That month is called the Marian month. It is in the month of May. In this month, many babies die at the hands of her baby Zeus, the demon of destruction, especially in maternity.

Excerpts from Ex Satanist Testimony Jean Paul Kalumba part 2

12/10/2023

ACHINYAMATA 24 PA 100 ILIYONSE AKUTULUKA CHIPEMBEDZO CHA CHISILAMU CHAKA CHILICHONSE PA DZIKO LONSE LAPANSI - ATERO AKATSWIRI AKAFUFUKU KU CHISILAMU

YESU KHRISTU ABWERA NSANGA

4. Ndiponso ndinamva mawu ena
kuchokera kumwamba akuti:
“ ‘Anthu anga tulukani, mwa iye,’
mungachimwe naye kuti musadzalandire
nawo gawo lililonse la miliri yake;

5. pakuti machimo ake awunjikana
mpaka kumwamba, ndipo Mulungu
wakumbukira milandu yake.
(Chivumbulutso 18:4-5)

24 PERCENT OF MUSLIM YOUTH ARE LEAVING ISLAM - MUSLIM SCHOLAR

Jesus Christ is coming.

Revelation 18:4

And I heard another voice from heaven,
saying, Come out of her, my people,
that ye be not partakers of her sins,
and that ye receive not of her plagues.

Heavenly NewsHub-INTEL

12/10/2023

ZA IMFA YA OYIMBA NYIMBO M'MALAWI NDI GUWA LA NSEMBE LA ILLUMINATI

MKULU WAKALE KU CHIPEMBEDZO CHA SATANA A TWAIBU AHAMIDU HAMIDI ALI AKULONGOSALAPO KULUMIKIZANA KWA INFA YA OYIMBA A CHICHEPERE MU INDUSTRY YA ZOIMBAIMBA MDZIKO LINO LA MALAWI.

INFA YACHITIKA POSACHEDWAPA MASIKU ANGAPO APITAWA NDI OYIMBA OTCHEDWA ATOT MANJE YEMWE ANAMWALIRA MWADZIDZI ATANGOTHA KUYIMBA PPA SHOW.

Heavenly NewsHub-INTEL

12/10/2023

KUIKA POYERA CHENICHENI CHIMENE CHIMACHITIKA KUMBALI PA MAUMBONI AMBIRI OMWE TIMAWAONA PA MA KANEMA A MAUTUMIKI ENA.

MA UMBONI OCHULUKA AKHALA AKUPITILIRRA KUBWERA POYERA NKUTSUTSA ZIMENE ADANENA KUJAMBULIDWA NKUONETSEDWA PA TV KUTI SIZINALI ZOONA KOMA AMAKAKAMIZIDWA KUNENA ZIMENE OJAMBULAO AMAFUNA KUTI ANENE.

TIKHALE TCHERU NKUSATENGEKA NDI MAUMBONI OWONERA PA TV, ENA SAKHALA OWONA.

MUDIKIRE UMBONI WENIWENI OGWIRIKA OSATI WA PA TV OKHA.

MUKAONETSETSA ANTHU AMBIRI AMENE AONETSEDWA PA KANEMA SIMUMAONASO MUKACHISIMO. AKATERO AMAKHALA KUTI ANACHITA KUWAPANGA HIRE NDIPO ABWELERA KWAO KAPENA ADAKHUMUDWA NDI UTUMIKIWO ATAZINDIKIRA CHOONADI CHIMENE CHIMACHITIKA POJAMBULA MA UMBONI. AMATHA OJAMBULAO KUWAKAKAMIZA KUNENA ZOMWE IWO AKUFUNA ZIJAMBULIDWE NKUDZAIKIDWA PA KANEMA.

NTHAWI ZAMBIRI ZIMENE ZIMALEMBEDWA PA PLACARD NTHAWI YA PRAYER LINE ZIMAKHALA ZABODZA POONJEZERA (EXAGGERATING YOUR REAL CONDITION) KUTI LIONEKE VUTO LALIKULU KUPOSA MMENE LILI.

MWACHITSANZO ULI BALA PAMWENDO IWO ALEMBA PLACARD YOTI IJAMBULIDWE PA TV KUTI UKUDWALA CANCER. AKAKUPEMPHERERA UKACHIRA AFTER SOME WEEKS ADZAPANGA PROGRAM YONENA KUTI MAN OF GOD ANAKUCHIZA CANCER ATAKUPEMPHERERA.

Heavenly NewsHub-INTEL

LAMULO LA CHIWIRI PA MALAMULO KHUMI A MULUNGU OMWE ANAPEREKA KWA MOSE, LILI MOTERE :AMBIRI SITIKULIDZIWA CHIFUKWA LIMABI...
12/10/2023

LAMULO LA CHIWIRI PA MALAMULO KHUMI A MULUNGU OMWE ANAPEREKA KWA MOSE, LILI MOTERE :

AMBIRI SITIKULIDZIWA CHIFUKWA LIMABISIDWA POOPA KUONONGA BUSINESS

[EKISODO 20:4-6]

4 “USADZIPANGIRE
chofanizira chinthu chilichonse
chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi
kapena cha mʼmadzi a pansi pa dziko.

5 USAZIGWADIRE
kapena KUZIPEMBEDZA, pakuti Ine Yehova
Mulungu wako, ndine MULUNGU WANSANJE ,
WOLANGA ana chifukwa cha tchimo la makolo awo
mpaka mʼbado wachitatu ndi wachinayi wa iwo
amene amadana nane.

6 Koma ndimaonetsa chikondi chosasinthika ku mibado miyandamiyanda ya anthu amene amandikonda, ndi kusunga malamulo anga.

12/10/2023
KODI BAIBULO LANU LIMATI CHIYANI PA ZA MUNTHU WA MOYO KUMALANKHULANA NDI ANTHU AKUFA? MZIMAYI UYU ALI MU CHITHUNZI YU AM...
11/10/2023

KODI BAIBULO LANU LIMATI CHIYANI PA ZA MUNTHU WA MOYO KUMALANKHULANA NDI ANTHU AKUFA?

MZIMAYI UYU ALI MU CHITHUNZI YU AMANENA POYERA KUTI AMAFUNSA NZERU ZOYENDETSERA MPINGO WAKE KWA MALEMU MAMUNA WAKE YEMWE ADALI ATAMWALIRA PA KANTHAWI.

BAIBULO LANGA KU KU BUKU LA DETORONOMO LIKUTSUTSANA NDI NCHITIDWE UWU MOLIMBA, KULANKHULANA NDI ANTHU AKUFA NDI MTUNDU UMODZI MWA MITUNDU YA UFITI.

TIYENI TIDZUKE KU CHINYENGO CHA SATANA CHOTERECHI.

DEUTERONOMO 18:9-14

9. Mutakalowa m'dziko limene
Yehova Mulungu wanu akupatsani,
musamaphunzira kuchita monga
mwa zonyansa za amitundu aja.

10. Asapezeke mwa inu munthu
wakupitiriza mwana wake wamwamuna
kapena mwana wake wamkazi ku moto wa ula,
wosamalira mitambo, kapena wosamalira
kulira kwa mbalame, kapena wanyanga.

11. Kapena wotsirika, kapena wobwebweta,
kapena wopenduza, kapena wofunsira akufa.

12. Popeza aliyense wakuchita izi
Yehova anyansidwa naye; ndipo chifukwa
cha zonyansa izi Yehova Mulungu wanu
awapirikitsa pamaso panu.

13. Mukhale angwiro ndi
Yehova Mulungu wanu.

14. Pakuti amitundu awa amene
mudzawalandira, amamvera iwo akuyesa
mitambo, ndi a ula; koma inu, Yehova Mulungu
wanu sakulolani kuchita chotero.

KODI KWA MZIMAYI UYU OTEROYU, TIKHULUPILIRE KUTIDI ZOPHUNZITSA ZAKE NZOCHOKERADI KWA MULUNGU?

SITIKULEMBA IZI POFUNA KUMBANA PA MTSUTSO WINAULIONSE OMWE UNGATULUKE PANKHANIYI AYI, KAMBA KA KUTI NDI NKHANI YA SERIOUS KWAMBIRI.
_______________________________________________

Necromancy is a form of magic or divination in which a person communicates with the dead, (as in The evil sorcerer used vile necromancy to get information on his enemies).
Necromancy can also refer to magic or witchcraft in general.

NECROMANCY.

"Necro " means death, while " Mancing " is derived from the word "romancing " and " Necromancy " means romancing the dead.

But when it comes to praying to the dead saints to find keys the way catholics do or talking to Saint Nicholas ( santa claus ) or people thinking they see apparitions of their dead family members in houses or mediums / psychics calling up dead relatives or people communicating with dead people through ouija boards are all demonic.

The Bible says communicating with demons like king Saul did when he tried to call up the prophet Samuel through the witch of Endor is an abomination to God in book of Deautronomy chapter 18

______________________________________________________________

9. When thou art come into the land
which the LORD thy God giveth thee,
thou shalt not learn to do after the
abominations of those nations.

10. There shall not be found among you
any one that maketh his son or his
daughter to pass through the fire, or
that useth divination, or an observer of times,
or an enchanter, or a witch,

11. Or a charmer, or a consulter with
familiar spirits, or a wizard,
or a necromancer.

12. For all that do these things
are an abomination unto the LORD: and because
of these abominations the LORD thy God
doth drive them out from before thee.

13. Thou shalt be perfect with the LORD thy God.

14. For these nations, which thou shalt possess,
hearkened unto observers of times, and
unto diviners: but as for thee, the LORD
thy God hath not suffered thee so to do.
(Deuteronomy 18:9-14)

(See also Leviticus 19:31, Leviticus 20:6, 2 Kings 21:6, and Isaiah 8:19)

Repent or perish. Repentace is a choice.

Heavenly NewsHub-INTEL

JEAN PAUL KALUMBA 1TESTIMONY OF A FORMER WIZARDBeloved, this universe is divided into two kingdoms. You got to know that...
11/10/2023

JEAN PAUL KALUMBA 1

TESTIMONY OF A FORMER WIZARD

Beloved, this universe is divided into two kingdoms. You got to know that planet Earth is divided into two kingdoms. Even the African continent is divided into two Kingdom. your country is divided into two kingdoms. That kingdom of light ruled by Jesus Christ and the kingdom of darkness ruled by the devil.

As a born again Christian, you must not be uneducated and uninformed about the kingdom of darkness. For you to combat the enemy, you must identify him. We must know about the origin of occultism and witchcraft that affect our lives.

You must not be uneducated about your opponent. You must know who you are up against. You got to know the enemy of your life, your wife and your children in order to shoot on target, not in the air.

As far as I am concerned, witchcraft is one of the worst things on earth because witchcraft prevents people from living God's destiny on earth, and it prevents people from maximizing and reaching their potential on Earth.

Witchcraft always targeted people from having God's promises and witches seek to shorten people's lives on earth through chronic diseases. That's why Prophet Isaiah 26:13 says, O LORD our God, other lords beside Thee have had dominion over us: but by Thee only will we make mention of Thy name.

Let me tell you in life, there are thrones established in people, lives, and families in countries by the kingdom of darkness in order to dominate and they are dominating in planet Earth. If you don't belong to Jesus, you are already dominated and you belong to the devil.

Even if you are a good guy, the fact that you don't have Jesus Christ you belong automatically to the devil and the Prince of Darkness is ruling in your life. He can destroy your work or your marriage.

If you are a Christian, you should make sure that the throne of your family is occupied by Jesus alone. Because there are powers establishing that throne over families and they are dominating and they are which is establishing their thrones over families and they are causing sickness and failure.

Therefore, a Christian has the obligation of praying for his family. In the book of Acts, chapter one, verse eight, the Bible say, you will receive power when the Holy Spirit comes upon you, and you will be my witnesses in Jerusalem, and in all Judea, and Samaria, and to the ends of the earth.

Beloved, Jesus said these words because He knew that on Earth, there were powers that were in operation and an activity power such as black magic, white magic, green magic, yellow magic, red magic, Roman Catholic magic, airpower magic.

Actually, after receiving Christ, I waited for seven years. I was in prayer and Bible study and after being taught and being filled with the power of the Holy Spirit then I began to testify. You cannot rush to war before being filled with the power of the Holy Spirit.

I will start this testimony by telling you how I was initiated into witchcraft. I am Jean Paul Kalumba and the fifth of a family of nine children. I am a father of five. My mother is alive but my father died some time ago. He used to be a member of the parliament in the Mobutu regime in 1981.

When I was in my fourth year in primary school, I had a friend who was a witch. We were really close friends. We were always together after school, and we were going to his place and my place to eat. And in the evening, we were parting on our ways and the following day in the morning, we were meeting again. Although we were good friends, I did not know his spiritual identity. You got to know who is your friend and his spiritual identity.

I noticed that in the class, my friend was never writing like everybody else. One day I asked him, "Why don't you write in a class like everybody." In response, he laughed louder and mysteriously. Then he put his hands on my eyes.

The moment he did that my spiritual eyes opened. And as a result, I saw the writing on the board, changing their meanings. Actually, these writings were insults. This was incredible. I even saw snakes on the board. I was about to shout in terror but my friend stopped me.

I was in terror and sweating and I could not tell my experience to my family as they were unbelievers. In fact, the opening of my spiritual eyes marked my initiation into witchcraft.

Witches traveled to their gathering place at 1 am. And when they do, many people get sick. It in that time babies cry in that time. Cats make strange noises. The person that discovered that I became a witch in the family was my auntie because she was a witch. She is the one who took me to the gathering of witches.

Actually, I was sleeping then I heard like something heavy landing on the roof. Then I saw my arms entering the house through the roof. She was naked. She then transported me to the astral realm of witches. When I arrived there, I got married to her in a ceremony. She was dressed in a white robe, and I was dressed in a black suit.

Later, we had our full moon, and we had s*x. Since that spiritual marriage, even my father began to notice that my auntie loved me more than her own children. My father could not understand what was her motivation. We had three children in the astral realm of witches.

But the following day at midnight, a paranormal event happened. There was a wind in my house blowing powerfully and the windows opened by themselves. I tried to knock in my father bedroom door to wake him up, but he was plunged in a deep sleep. Actually, there was an entity coming from the realm of the world of the cemetery. That's why there was this wind.

Then I saw a white woman appearing before me, even though the doors were closed and there were bodyguards outside. She was a siren from the realm of the cemetery.

She said her name was Madame Lanow Viera. This demon could afford to get in our house, because just Christ was absent, so the family was insecure, defenseless and exposed. Then the evil spirit from the cemetery asked me to travel with her.

Actually, she was shooting lasers from her eyes. Then I did an astral traveling with her to a place but I don't know specifically where it was. I could hear noises of birds and animals.

Then she took a knife and she injured herself and she told me to drink my blood. But I refused. And I tried to run but in a split second, she was in front of me, and she then forced me to drink her blood.

And while I was drinking her blood, I felt like I was losing my humanity and a demonic force and energy was entering me. Afterward, she asked me, "Are you feeling something in your stomach?" Then I felt like vomiting and then I started to vomit.

Then a lizard came out of my mouth. The lizard started to get bigger and bigger and it reached a length of six meters. The siren told me to seize it on the neck, which I did. Then the lizard became little. As it got little, the siren asked me to swallow it again, which I did.

Then she said to me, this is the spirit of cannibalism in you. Every time you are beaten, the lizard is going to feel the pain for you, but at 6 pm you will feel that pain. This was difficult for me. And since then, when I was angry, my eyes were getting red blood and my nails were growing longer and to calm myself I had to bite someone on his neck like a vampire.

That night after the ritual with the siren when I woke up there was blood on my mouth. My elder brother noticed it and he went to call my father but when he came with my father the siren Helen removed it from my mouth already.

This night marked a significant and fundamental change in the family because there is now an agent of the devil in the family, a committed witch but no one in the family knew about it as they were all unbelievers.

Actually, in school where I contracted witchcraft, there were three categories of pupils. The first one like everybody else, go there to study and prepare the future in order to have a better life. The second category also comes to school to study for the future. But they have an assignment from the dark world which is to destroy pupils who came to study.

Usually, during the break, they give fellow pupils their food in order to destroy them or to initiate them into witchcraft. But if you serve God, He will keep your child in school against witchcraft initiation which is like targeting and initiating children in sorcery as they are innocent.

So when you give birth to the baby, the first thing you have to call the pastor to cover the baby with the blood of Jesus because people would want to visit the baby including witches. When witches come to visit the baby they will shoot a ray of light to the baby navel in order to initiate the baby and do witchcraft.

So a baby needs to be protected. In fact, witches from their third eyes can see the start or the destiny of the baby. That's why when Jesus was born the first people to know that a Great King is born were astrologers.

They said, "We saw His star," and today we have witches functioning like astrologers. They are checking babies, stars and destinies and they are combating and trying to get a hold of babies' destinies. That's why when you are taking the baby to the church, do it with an effort.

The devil likes the initiation of babies because if a baby was supposed to live at two years on Earth, he might live that day two years in practicing witchcraft and his service.

The third category of students come from the Slavic world which is the kingdom of Rosicrucianism in the infernal Kingdom ruled by a hybrid demon called Bernard.

These people are wealthy and intelligent, they have good cars and money, people envy them. They come to the university to initiate students into Rosicrucianism.

Firstly, let me define what is a witch. A witch is someone who has surrendered his spirit to the devil and he has opened his life to be inhabited by a demon who influenced him to commit crime and works of wickedness.

This demon, transmit the sinful lifestyle driven by wickedness in order to commit crimes. A witch is prepared for his task in the astral world, which is to offer human sacrifice to Satan. Witchcraft is an exotic branch of black magic, which is wicked, destructive, devastating, and murderous.

The moment you become a witch, you must offer a human life as a sacrifice, and once the sacrifice is offered, the hierarchy will take one bone from the victim and design a mystical phone for the initiate and they will take another bone from which they will design a camera for the initiate to monitor his target and family and from another bone, they will design a seat for the initiate in the assembly of the witches.

After being initiated in witchcraft I was given a new name. In the physical world, my name is Jean Paul but in the spirit realm of witches, I was named PBT and that's the name they were calling me over there in the astral realm of wizards.

Beloved, when you are exorcizing a witch, he must tell you the name of the person who initiated him and his own name in the world of witches. He also has to tell you about his function in the world of witches, and how many children he has in the realm of witches. You should ask him what is his phone numbers in the astral realm, and you have to ask him which animal is his character.

In fact, there are three types of witchcraft. There is first, subconscious witchcraft. In this case, the person is unaware that he is a witch, they are using him they are even using his face too but the witch is another.

The second level is the conscious witch. He is committed witch. He knows consciously that he is a witch. He has a specific function and has a grade. He is an active witch. If he is a man, he will be forced to marry in the world of witches. If she is a woman, she will be taken into a marriage without her consent.

If she is a mother, she will have to marry one of her own sons in order to use them. Obviously, she would love that son more than other children. And when the boy grows up and gets married, he will love her mother more than his own wife.

He will be closer to her mother than his wife, and it will be her mother running his household because the man is married and used by his mother and they are giving birth to children in the astral realm.

This mother will be coming in the night to mo**st her daughter in law using the p***s of a dog. The victim will dream that she is having s*x with a man but it's the mother in law in activity. As a result, the victim will suffer a miscarriage.

In this scenario, you are dealing with a committed witch who consecrated his life to work for the kingdom of the devil. Usually, the devil uses active and committed witch in the church and uses them as an infiltrator to occupy a strategic position in the church in order to cause chaos among the children of God.

Normally, before giving responsibility to anybody in the church, pastors must pray and hear the voice of the Holy Spirit to avoid a fatal mistake.

The third kind of witchcraft is called blood witchcraft. There are people who are born witches, and they have witchcraft in their blood. And when they married, they give birth to children who are witches. We are dealing with hereditary witchcraft.

Let me warn you, women, not to allow just anybody to breastfeed your baby. Actually, if the person breastfeeding your baby is a witch she can transmit the baby witchcraft and when a baby contract witchcraft you will notice that she will fail to develop properly and you will notice that only the head that is growing in size as if the baby has a deformity.

After initiation in witchcraft, I was supposed to go through totemization like every witch. Totemization is done through ritual and ceremony in which there is a demonic presence. What happened in totemization, I will choose an animal as a totem. I chose a cat.

Afterward, I wrote my name on a paper and I threw it in a fire. Then I was given the heart and blood of a cat to swallow, which I did. Then I declare publicly that I was not Jean Paul Kalumba. I declare that I was a cat because that is the animal that I chose as Totem.

Other people choose a lion, or leopards or tiger and as the ceremony was attended by a demon, the behavior or the characteristic of a cat was infused in me. Consequently, I will be manifesting the feature of a cat because I am inhabited by the spirit of that animal, and I will manifest the image of the animal even in my movement and my behaviors.

And the demon responsible for totemization is called Shiva, the Lord of the Flies, He is a prince of darkness. The devil gave him the power to remove the image of God in men and replace it with animal nature. He put down animals image in humans.

Every witch that goes through totemization and when a which is about to travel in hyperspace, he will return to his totemic animal then he will use it as a tool to travel space.

After totemization, if I had children in the physical realm, I would have been given a seed to plant behind my house. As a result, a spiritual tree would have grown behind the house, and that tree would produce a specific number of fruits.

I mean, if I had 10 children, the tree would produce 10 fruit, but every year there will be a wind blowing on the tree and the fruit will fall from the tree. As a consequence, one of my children would have died and this would be happening every year. That wind would be blowing every year until all the fruit fall and all the children die.

When witches attended night meeting, the first report that they present is that of their families. Every witch has to report everything happening in his family. As a result, there will be blood, conspiracy, and schemes against their families. There will be rituals, dancing and cursing in order to hinder their family progress.

I always said that one of the foundations of Christian life is morning prayer. Because throughout the night witches just spend time in conspiring and plotting against the children of God, and they designed schemes in order to attack them, but with morning prayer, you can undo everything. You can render powerless their plot.

The morning prayer is a massive weapon against the eight hours of night activity of witches and occultist and there is a lot of power in morning prayer service. In every family, the devil is working to place a witch as a representative who will serve as a transmitter of information about the family in the dark world.

In the second world war, the Americans were using a plane called flying fortress in order to capture details data about the enemy. In witchcraft, a fortress is a human. I mean, a witch from which all information about the family is transmitted to the dark world. Consequently, they will plot and conspire to hinder the family.

As a witch, I was transforming myself into a cat and I was getting the information about my family and I was reporting them to the astral realm. I was the cause of sickness in the family. I was doing this when people are paid their salary so that they spend them in the hospital.

After being initiated into witchcraft by my best friend, I ended up with another friend who was also in the occult. He told me that he will do a demonstration in school, but I must be strong. When we arrived at school, he started to sing in Arabic. As consequence, our class Blackboard changed. Then everybody saw a spirit writing on the blackboard. He was writing the sentence, I am looking for Marie Tree.

When the students saw that an invisible person was writing on the blackboard, they panicked and they ran out. Later I heard that this incident is happening in all the Catholic schools in the city. This evil spirit was terrible.

The city was in turmoil and all the schools closed. People even died because of this spirit who came from the cemetery to manifest in the city. It was a demon deployed by my friend. He managed to shake the whole province by deploying a demon of the cemetery in schools.

Then the authorities sought help from a Catholic priest to resolve this situation. That priest did not use the name of Jesus, but he put on a gun and having kabbalistic symbols. These symbols are called satanic ventricles by the Roman. These kabbalistic signs in the priest garment represent a demon called Christ the King.

Actually, the Roman Catholics don't worship the same Jesus as Christians because, in white magic, they are three Jesus. The first Jesus is called Christ the King. He is a false Jesus, he is venerated on the 25th of November. He is a demon of the world of the damned. He is not the Jesus Christ of Nazareth who came back to life.

The second Jesus is called Jesus of London. He is the demon who gives successes to businessman, sportsman, and musicians, people invoking for success. And many Congolese musicians mentioned him in their songs.

The third Jesus is called Jesus of Africa. Over here in Katanga, there are places you can see his footsteps as people go there to watch them.

I was saying that the priest was wearing a garment having kabbalistic signs. When he met that demon, the demon submitted to him to honor him. The truth about witches is that when they cannot defeat you in a spirit realm, they will proceed in the physical realm. They will try to upset you or to get you angry, either by their actions or their words. It's when you get angry that the door is opened that a shortcut is made for them to enter you.

Continue from part 2

Address

Masauko Chimpembere Highway
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Heavenly NewsHub-INTEL posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share