Fresh Media

Fresh Media Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Fresh Media, Media/News Company, .

24/03/2026

Kuwumira ndi khalidwe labwino and lopindulitsa osamachita Nako manyazi

Basitu Pa mpanje pano tupanga kaye izi
20/03/2026

Basitu Pa mpanje pano tupanga kaye izi

Current situation at Domasi
17/03/2026

Current situation at Domasi

Komatu ngat zikwama zake zili izi BiiiiiiWati muli Chani koma
17/03/2026

Komatu ngat zikwama zake zili izi Biiiiii
Wati muli Chani koma

Did You Know? 🇲🇼🎤Mu music industry ya ku Malawi, ma diss nthawi zina amathandiza kuti artist  odisayo azitchuka,  makama...
17/03/2026

Did You Know? 🇲🇼🎤

Mu music industry ya ku Malawi, ma diss nthawi zina amathandiza kuti artist odisayo azitchuka, makamaka ngati pali influence from ma big names mu industry omwe amafuna wina azidisidwa kwambiri.

Eyaaa Inu kungoti sizimayendera aliyense.

Tawonapo ma new artists akuyesera kudiss ma big names, koma nyimbo zawo osahita or iwo amene kunyozedwaso, kumaiwerenga ma upcoming Inu Kuma kumatenga mbali ndithu imakhala support yanu ngat ili ndi influence ya mphamvu.

Ku Malawi Nkhani, si diss song koma who is backing the noise.

Inu mukuti bwanji? 🔥🎶

16/03/2026

Mukawonetsetsa bwino bwino pa social media pano ambiri tupangapo fake life 😅

Zakayu content yake inali ya bho when he was criticizing a group of people not munthu m'modzi. Honestly zinasanduka ngat...
15/03/2026

Zakayu content yake inali ya bho when he was criticizing a group of people not munthu m'modzi. Honestly zinasanduka ngat zotumidwa za azimayi zeneni zeni🚮🚮

08/06/2024

Koma Jetu Mw 🤣💔
A Malawi tivutika🤣

Address


Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Fresh Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share