Dope kid

Dope kid This is official page for Dope kid
*Artist
*Music Producer
*Entrepreneur
(1)

Komatu a Pakaya Tv  mumamupezelela Mbayani King akachita matako Ngati fosholo ๐Ÿ™Œ๐Ÿ˜‚
15/05/2026

Komatu a Pakaya Tv mumamupezelela Mbayani King akachita matako Ngati fosholo ๐Ÿ™Œ๐Ÿ˜‚

15/05/2026

Gwamba better ija unakunga
ase nyimbo yachilimbikiso

12/05/2026

Fredokiss ๐Ÿ”ฅndaiyamba Yama suit ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅntchana to the world

11/05/2026

I have an idea Nditati ndapeza 2 million nkuipanga invest Kuti ndisegule studio ndigulile equipments yoyambila koma ya quality yabwino nkuwafikila ma producers akulu akulu oti ndikamalizeko kupanga mastering music production Kwa mezi iwili nkuisegula mu gettho starting with ka fee kongothandizana basi Kuti tizitoleleso nkupeza katundu wa classic nsogolomu sizingatheke kukhala otukuka nkuisegula music company and other business?

๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡
*Computer yamphavu :500k -700k
*Audio interface+ mic 400k - 600k
*Ma monitors+ head phones 300k -400k
*Daw+ plugins and producer who can teach us 100k - 200k
Back up yamagesi.50k - 100k
Rent fee 3 months : 150k
Note : ndi example chabe iyi โ˜๏ธ๐Ÿ‘†โ˜๏ธ

Imagine session fee nditayamba with 15k beat voice 15k voice titati pasiku kukubwela anthu 5 ozapangisa ma beat or ozapanga recording 15k x 5 ndekuti pa day titha kumapeza 75 pin pa day kumachosapo 10k 5k for food 5k magesi ndekuti patha kumasala 65k kuponya kuthumba izizi kuzipanga Kwa 30 days 65000 x 30 = 1950000 million Inu pakutha pachaka sitingakhale chimodzimodzi Apapa titha kukhala tapita basi ndi yathu ya farming ija eeee ngozi.

Ku malawi ndalama ziliko tingophunzila kupangana support , tisiye kuchitilana nsanje, osamakonda zaulele coz mostly chaulele sichikhala cholongosoka kweni kweni zimakhala za temporary we need to start with small ma incomes azibala zipaso zinzake.

Stay blessed

06/05/2026

Beyond the arguments, itโ€™s just really sad that most people in this country, from kids to adults, canโ€™t and donโ€™t read. Literacy is so essential to a dignified and intelligent life, and there used to be a national push for it not too long ago. And now itโ€™s damn near gone.

02/05/2026

Kumalimbikila nyumba zathu izatimangile Mzati Construction Limited awawa nde ndilibe nawo mawu

Gwamba  ase kunotu kuli uyu tinaziwana kumowa 2018 guy oziwa kucheza kuchokela mom'mo mangoti Gwamba nzake wa Charisma M...
01/05/2026

Gwamba ase kunotu kuli uyu tinaziwana kumowa 2018 guy oziwa kucheza kuchokela mom'mo mangoti Gwamba nzake wa Charisma Madness ๐Ÿ™Œ๐Ÿ˜‚

30/04/2026

The way I love my n***a Fredokiss it's a special love from God ๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dope kid posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Dope kid:

Share