Mponda circle

Mponda circle Funny stuff, sports, Animals and many more

29/04/2025

Ace Jizzy BASOPOπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Lero Hip hop ilowe m'bwalo.   Ace Jizzy  mutinyamula??? 😒πŸ˜ͺπŸƒπŸƒπŸƒπŸƒπŸƒπŸƒ. Achina Gattah Ase  and 1000 others are waiting patient...
28/04/2025

Lero Hip hop ilowe m'bwalo. Ace Jizzy mutinyamula??? 😒πŸ˜ͺπŸƒπŸƒπŸƒπŸƒπŸƒπŸƒ. Achina Gattah Ase and 1000 others are waiting patiently

Ndikawawona ndimangoti Kasongo yeyeπŸ˜‚πŸƒDr Michael Usi
27/04/2025

Ndikawawona ndimangoti Kasongo yeyeπŸ˜‚πŸƒ
Dr Michael Usi

Anthu sakuyakhula bwinoyiπŸ˜‚πŸ˜ͺ
26/04/2025

Anthu sakuyakhula bwinoyiπŸ˜‚πŸ˜ͺ


25/04/2025

Timpepherere phwedo

Timpepherere phwedoi
25/04/2025

Timpepherere phwedoi

   #Anthu ochuluka afika ku bwalo la magistrate la Lilongwe kumene akufuna kudzanva mlandu wa Tumpe Mtaya amene amatchuk...
24/04/2025


#

Anthu ochuluka afika ku bwalo la magistrate la Lilongwe kumene akufuna kudzanva mlandu wa Tumpe Mtaya amene amatchuka ndi dzina lakuti Phwedo.

Phwedo amene wasintha zovala ndipo ali mu suit, walowa m'bwalo la milandu koma ndiye kunali ntchito.

Bwalo limene mumalowa anthu osaposera makumi awiri, munalowa namtindi wa munthu pamene munali mlandu wina.

Apa zinatengela mphanvu za anthu ogwira ntchito ku bwalo la milandu kutulutsa likukumweli kuti mlandu winawo upitilire.

Anthuwa anapitilira kuchita phokoso koma zinatengela mau a Kendal Kamwendo amene anawapempha kuti asunge bata.

Pakadali pano bata labwelera ndipo mlandu winawo ukupitilira

Olemba Lucy Kadzongwe, Lilongwe.


24/04/2025

Morning family

Mandala, madala SopanoπŸƒπŸ˜ͺ
23/04/2025

Mandala, madala SopanoπŸƒπŸ˜ͺ

11/03/2025

Kumenya kugwetsa kuja mumatathauza izi etπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜€πŸ˜œ

Address

Mangochi
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mponda circle posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share