01/09/2025
2014 -2020
GDP Growth: chuma cha dziko chinakwera pafupifupi 4% โ 5% ngakhale nthawi zina chinatsika.
Inflation: inakwera kwambiri mu 2015โ2016, koma mu 2018 inatsika kusonyeza kuti mitengo sinali kukwera kwambiri komanso kwacha sinagwe kwambiri.
Inflation inatsika kuchokera pa 24% kufika pa 9.4%.
Poverty: Malawi inali pa number 3 pa ndandanda wa maiko osauka kwambiri padziko lapansi.
70% a Malawi ankakhala osauka (amakhala pa $1.90 patsiku).
Sources: World Bank, IMF, Reserve Bank of Malawi
2020 - Pano
GDP Growth: mu 2020 inatsika mpaka 0.9% chifukwa cha Covid-19, kenako inapanga recover pangโono 2.6% mu 2021 ndi 1.7% mu 2022.
Inflation: inakwera kwambiri, 25% mu 2023 โ yomwe ndi yokwera kwambiri mu zaka zoposa 10.
Ngongole: ngongole zakunja zidakwera kufika pa 56% ya GDP mu 2023.
Forex & mafuta: kusowa kwa ndalama zakunja ndi mafuta kunawonjezeka kwambiri.
Sources: IMF, World Bank, Malawi Macro Poverty Outlook
Conclusion
2014โ2020 : Inflation inatsika kwambiri, GDP inkakula pa avareji yabwino, koma Malawi inakhalabe mโmayiko osauka kwambiri padziko lonse.
2020โ: Chuma chinakhudzidwa ndi Covid-19, ngongole zambiri, inflation yokwera, komanso kusowa kwamafuta, zomwe zinapangitsa kuti zinthu zikhale zovuta kwambiri kwa anthu ambiri.
Note: The insight siitenga mbali pa ndale koma chilungamo chokha
Pali zambili zofuna kusintha mu dziko lino osangoti atsogoreli.
What's your comment?