
08/09/2025
Mu hood mumabeba yeah/
Asikana akavala zopita mphepo akatchena/
Anyamata akaponya zopanda mikono zimanveka/
Sife tokha sife tokha/
Ma chick so amaspota/
Remember paja mzotheka/
Imakhala summer yabeba/
Imakhala summer ya tentha/
Kunyanja wamame panchenga/
Naponyerana oh napreza/
Nagemurana so naseka/
Momwe akhalira macheza