Podcast Balaka

Podcast Balaka Analysing Every Hot News.........

Mtsogoleri wa UTM Dr. Dalitso Kabambe wasankha Dr. Mathews Mtumbuka  ngati wachiwiri wawo pachisankho chikudzachi.
27/07/2025

Mtsogoleri wa UTM Dr. Dalitso Kabambe wasankha Dr. Mathews Mtumbuka ngati wachiwiri wawo pachisankho chikudzachi.

A Kondwani Nankhumwa asankha a Bertha Mackenzie Ndebele — yemwe kale anali phungu wa dera la kumadzulo kwa Boma la Balak...
26/07/2025

A Kondwani Nankhumwa asankha a Bertha Mackenzie Ndebele — yemwe kale anali phungu wa dera la kumadzulo kwa Boma la Balaka — kukhala wachiwiri wawo pachisankho cha pa 16 September.
Izi zachitika patangodutsa masiku ochepa kuchokera pomwe a Ndebele anapereka makalata owatsimikizira kuti ayima ngati phungu m’dera la Balaka West.

 In a surprising turn of events, DPP presidential candidate Arthur Peter Mutharika has unveiled former Malawi Electoral ...
25/07/2025



In a surprising turn of events, DPP presidential candidate Arthur Peter Mutharika has unveiled former Malawi Electoral Commission (MEC) Chairperson Jane Ansah as his running mate in the upcoming presidential election. The announcement has stirred mixed reactions across the country. Supporters hail the move as a return of seasoned leadership, while critics recall the controversies that marked Ansah’s time at MEC. As the election draws near, Malawians are watching closely.

Will this duo win public trust?

25/07/2025

We are more than a podcast,We are a movement 🔥

24/07/2025

📢 LERO! LERO! LERO! 📢
TIMES Radio & TV Station ili ku Balaka Stadium m’mawa uno pa 8:00 AM! 🎥📻

Akudzajambula ma program achinyamata monga:
🎭 Masewero
🎤 Nyimbo (Oyimba)
📝 Ndakatulo
💃 Ovina
✨ Ndi ena ambiri!

ZONSE NDI ZAULERE!

Tikuitana achinyamata onse omwe ali ndi luso kapena kuthekera kuti abwere kudzawonetsa maluso awo.
Ichi ndi mwayi waukulu wodziwika pa TV ndi Radio!

📍 Malo: Balaka Stadium
🕗 Nthawi: 8:00 AM

Musaphonye! 💥

23/07/2025

MAN to MAN: When your woman is not around, open her lotion, add a little water, and shake it well. Times are tough—everyone has to manage! 🤧

Good morning 😅

Mukuyembekezera Zotani loweruka lino ?
22/07/2025

Mukuyembekezera Zotani loweruka lino ?

Catch our very first episode this coming Saturday.We sit down with Charles Sinetre for a powerful conversation you won’t...
21/07/2025

Catch our very first episode this coming Saturday.
We sit down with Charles Sinetre for a powerful conversation you won’t want to miss.

🔥 Insightful. Inspiring. Unmissable.


12/07/2025

A Memorial Mass in honour of the late Lucius Banda — he lived with purpose, he saved and today, we remember him.

Address

BALAKA
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Podcast Balaka posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share