Oga Titus

Oga Titus Content creator, political analyser and Business man
(1)

23/07/2025

Fake prophets😂🙌

23/07/2025

😂🙌

22/07/2025

Amalawi ati mumvese bwinobwino 🤣

21/07/2025

Someone mistakenly called my phone today thinking I’m his boss and begged for 2 days off work and I gave him 1 month off 😂😂

21/07/2025

Nkhani ija yamufika munthu wamkulu🤣🙌

21/07/2025

Ching'aning'ani come and see your uncle 🤣

21/07/2025

Inock Chihana kuwafusa amalawi kuti anene zomwe akufuna❤️🤝

Koma ichichi amwene🤣🙌
20/07/2025

Koma ichichi amwene🤣🙌

Nkhani ija yawafika anzathu aku Maula Prison 🤣🙌
20/07/2025

Nkhani ija yawafika anzathu aku Maula Prison 🤣🙌

20/07/2025

Nkhani ya manifesto ija yamupeza The DC Mwana Oopsa kwambiri 🤣🤣🙌

Masamu🫢New Born bay = 500 thousand Kwacha Number of new born babies in Malawi latest Data =1878 GDP Malawi =11.01Billion...
20/07/2025

Masamu🫢
New Born bay = 500 thousand Kwacha

Number of new born babies in Malawi latest Data =1878

GDP Malawi =11.01Billion USD

Calculation

500 thousand Kwacha x Ana 1878= 939 million pa Tsiku yopasidwa ana

Pachaka masiku 365 x 939 million Kwacha = 342.7 Billion Kwacha pa chaka

Pa Zaka 5 ndiye 342.7 Billion x 5 = 1.7 Trillion Kwacha

Ndiye kuti 16% ya Chuma cha Dziko lino kupasidwa kwa ana obadwa Dairly

Apapa investment establishment costs palibepo , operations costs palibepo , processing costs palibepo,

✌️✌️✌️✌️✌️😭😅 THIS IS BODZA

MLEMBI WA MANIFESTO WAPEZEKA😂1. Mpikisano obeleka pomwe 500 sauzande kwacha pa mwezi pa mwana obadwa aliyense2. Zimbuzi ...
20/07/2025

MLEMBI WA MANIFESTO WAPEZEKA😂

1. Mpikisano obeleka pomwe 500 sauzande kwacha pa mwezi pa mwana obadwa aliyense

2. Zimbuzi zogujumula kapena kuti zofulasha masukulu onse mdziko la Malawi

3.Kulemba ntchito anthu okwana 3 Million

4. Kumanga Kamuzu Stadium 🏟️ komanso Mzuzu Stadium zamakono

5. Kumanga city yamakono ku Chipoka

Address

Mzimba

Telephone

+265888518802

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Oga Titus posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share