Abule Creations

Abule Creations Timajambula ma Audios ndi ma Videos pamitengo yabwino try us simudzakhumudwa

Tichite Mongokumbusana k*t ngat mukufuna kupangisa ma ARTWORK Abwino, kaya muli ndi CHINKHOSWE , ma UKWATI tingoti choch...
01/03/2025

Tichite Mongokumbusana k*t ngat mukufuna kupangisa ma ARTWORK Abwino, kaya muli ndi CHINKHOSWE , ma UKWATI tingoti chochitika chilichonse chomwe inu mungafune VIDEOGRAPHER , ngakhale k*tsatsa MALONDA anu tipezeni ife tikupangile pamintengo yabwino.
Ndipo nkhan yabwino ndiyosangalasa ndiyak*t tili ndi PROMOTION munyengo imeneyi yomvuta zithuyi, posafuna k*t musafinyike kwambili tabwera ndi PROMOTION imeneyi yomwe tangotsisako mintengo ya zithu zathu ndipo zili motere:

VIDEO SHOOTING AND EDITING "Single"
kuchoka pa 80,000 tsopano ili pa 65,000

Ikakhala gulu la choir "Single" kuchoka pa 100,000 tsopano ili pa 85,000

EP ARTWORK, COVER DESIGN, SURFACE DESIGN,
Kuchoka pa 35,000 tsopano ili pa 25,000

MA NORMAL ARTWORK
Kuchoka pa 25,000 tsopano ali pa 15,000

UPLOADING
Kuchoka pa 30,000 tsopano ili pa 15,000 kwa 1 week

Kukakhala k*tsatsa malonda anu pama platform athu kumeneku sitinagundeko chifukwa kulibe ntengo weni weni wokhazikika, ndizongokambilana bas malingana ndi business yo k*t ndiyotani.

Promotion yi inayambika pa 1 February 2025 ndipo izatha pa 30 June 2025
Uwu ndimwai wamzama ofukula ndimanja nkhasu lilipo

Mukafuna kudziwa zambili call/WhatsApp pa 0889925656 kapena tipezeni ku inbox.

OSAIWALA KUPANGA LIKE AND FOLLOW FACEBOOK PAGE YATHU, K*T ZAMBILI ZISAMAKUPHONYENI

TANGODINANI APA πŸ‘‡
https://www.facebook.com/profile.php?id=61571304070047

Or apaπŸ‘‡
https://www.facebook.com/profile.php?id=100069856988174

Kwa amene mumamutsata bwino L**ENI JASI Nyamata waku Dedza pa Linthipe 1 yemwe mu music industry amadziwika ndidzina lot...
01/03/2025

Kwa amene mumamutsata bwino L**ENI JASI Nyamata waku Dedza pa Linthipe 1 yemwe mu music industry amadziwika ndidzina loti L**E GEE

Muchaka chino cha 2025 iye pokhala upcoming artist sakubwelera mbuyo kapena kufooka kom kuonesera poyera luso lomwe alinalo ndikunena pano wabwera ndichinyimbo chatsopano chomwe mutu wake ndi
"MINYAMA"
Nyimboyi waimba mothandizana ndi Jahmin

Chomwe akufuna kwainu amalawi ndi support yanu powalandila iwowa monga ma upcoming artist
Apangeni like/follow pa page yawo πŸ‘‰ **E_JASI_WOIMBA_WAMAWA

Zanyimboyi nde tiyeni ku YouTube komanso m***a kuipeza pama platform onse

MUKAFUNA MA ARTWORK ABWINO KOMANSO KUPANGA NAFE BUSINESS TIPEZENI KU PAGE YATHU
πŸ‘‡

TAMVAN IZI 🚨Apolisi kuno ku Zambia amanga Mayi wazaka 51 Sylvia Mutoba Kalaba pamodzi ndi ana ake kaamba koti mnyumba mw...
16/01/2025

TAMVAN IZI 🚨

Apolisi kuno ku Zambia amanga Mayi wazaka 51 Sylvia Mutoba Kalaba pamodzi ndi ana ake kaamba koti mnyumba mwawo mwapezeka thupi lakufa la mwamuna wawo yemwe wakhala akusowa kwa zaka pafupifupi ziwiri.*

Malingana ndi nyumba ina yowulutsa mawu ya Diamond, yati mchimwene wa malemuyu Emmanuel Kalaba wauza apolisi k*ti iwo ngati akubanja akhala akusakasaka m'bale wao ndipo mayiyu amakaniza anthu kufika ku nyumbayi.

Zadziwika k*ti malemu wa ndi a George Kalaba, omwe anali osewera mpira wakale wa timu ya Zanaco.

Malingana ndi mneneri wa apolisi Rae Hamoonga, wati k*tsatira kafukufuku iwo anakwanitsa kupita ku nyumbayi komwe anapeza khomo lotseka koma anthu ali mkati, ndipo atalowa anali odabwa kupeza thupili litasala mafupa okha pa k**a m'chipinda china.

Ndipo pakadali pano, apolisiwa akusunga muchitokosi mayiyu Sylvia Kalaba, azaka 51, pamodzi ndi ana ake anayi omwe ndi Natasha, 19, Sandra, 22, Wendi, 27, komanso mwana wina wa zaka 15 ndipo kafukufuku ali mkati pofuna kuziwa zambiri pa nkhaniyi.

πŸ‡ΏπŸ‡²

13/01/2025

Morning

11/01/2025
02/01/2025
Zabwino zonse kwa inu nonse amene mwalowa nawo muchaka chino cha 2025Mulungu anakhala okhulupilika muchaka chonse cha 20...
01/01/2025

Zabwino zonse kwa inu nonse amene mwalowa nawo muchaka chino cha 2025
Mulungu anakhala okhulupilika muchaka chonse cha 2024 potiteteza, ndik*tipasa chisamalilo chabwino potipambanisa muzithu zomwe patokha sitikanatha k*thana nazo.
Panali zotsamwisa zambili koma mulungu sanasamale zonsezo kom kungoonesesa k*t umoyo wathu uli bwino kufikila lero pomwe taonanso chaka chino (2025) kumwamba kudyere nyama πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™

01/01/2025

Kamtengo wezi bas
Khalani otsogola popeza nawo katundu wabwino uyu pamintengonso yaziii

Address

Chilimba
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Abule Creations posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share