16/07/2025
BENGO KUKONDA KUPALAMULA๐
Bengo anali muthu okonda mikangano, tsiku lina analowa mu sitolo ina mtawuni ndipo anaganiza zokagula chingambwe, atafika anachedza motere;
BENGO: muli ndi fodya wachingambwe?
MWIN STORE: ayi stimagulitsa fodya wachingambwe .
(Tsiku lina)
BENGO: muli nd fodya wachingambwe?
MWINI STORE: Iwe ndidakuwuza kale k*t stimagulitsa fodya wachingambwe muno!! ukadzabweraso ndi funso limeneli ndizakukhoma nd hamala.
(Tsiku Lina)
BENGO: muli ndi hamala ?
MWINI STORE: Ayi tilibe.
BENGO: Nanga misomali?
MWINI STORE: Tilibeso.
BENGO: Muli nd fodya wachingambwe?
MWINI STORE: ???