Malawi Daily

Malawi Daily To be proud of learning is the greatest ignorance🤐
(1)

19/06/2026

Big shout out to my new rising fans! Nyakwawa Wa Mikuya, Zai Bieb, Andrew Mtemela, Ackim D Chidzan, Do Bentos De Benman

19/06/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Chisomo Lalanna Chikazingwa, Dick Mapondo, Peace Man, Evangelist Andile Nyaba, Gogo Chinyama

Pano chili pa Banja😃😃
19/06/2026

Pano chili pa Banja😃😃

19/06/2026

Malawi Daily
Whatsap Group👇

Nkhani yomwe inakula masanawa inali ya nzimayi yemwe anatseka ndege koma sakudziwika. Dedza Kasina:" Mwati panali nzimay...
19/06/2026

Nkhani yomwe inakula masanawa inali ya nzimayi yemwe anatseka ndege koma sakudziwika.

Dedza Kasina:" Mwati panali nzimayi wina wachisilikali yemwe anatseka chitseko cha ndege? "

Gripps Chimzimu:"Eya ndi amene anatseka."

Chair Nyamilandu:" Omaliza kukwera ndege anali ndani? Anatseka chitseko ndi ndani, may you confirm."

Gripps Chimzimu: "Nzimayi ndi yemwe anatseka chitseko."

Chair Nyamilandu: "Anali pa passenger list?

Gripps Chimzimu:" Ayi sanali pa list yathu, anali pa list ya ma Crew Members. "

Dedza Kasina: "Munati ma pilot sanatsike ndege nde anatsekayu ndi ndani? Uniform yake inali yotani?"

Gripps Chimzimu:"Anavala uniform ya Blue yosonyeza kuti ndi ogwira ntchito mommo."

Mwanza Central:"List ya ma passengers onse muli nayo? "

Gripps Chimzimu:"Yes, list tili nayo."

Lilongwe Mude: "Kodi ndi Gloria Kamtukule kapena ndani? Inu apapa mwalemba Gloria Mtukule, mwati anafika nawo ku Airport."

Gripps Chimzimu: "Ndi yemweyu, Gloria Kamtulule, Mtukuleyo tinalakwitsa polemba.

Chair Nyamilandu:" Kodi panali katundu yemwe anayikidwa mu ndege? Anayika ndi ndani?

Gripps Chimzimu: "Mr. Chair panalibe katundu yemwe anabwera in advance ,katundu yemwe anabwera ndi mdipiti wa a VP."

Chair Nyamilandu: "Pali chilichonse chachilendo chomwe munaonapo pa tsikuli?"

Gripps Chimzimu: "Ayi panalibe, kumva kuti ndege yakanika kutera sichachilendo, tazionapo nthawi zambiri."

Zomba Thondwe:Katundu wa a VP anadutsa pa scanning machine?"

Gripps Chimzimu: "ayi analowa straight ndi a ADC sanadutse pa machine."

Dedza Mayani: "Yemwe amasunga ma key a ku VVIP anali ndani?"

Gripps Chimzimu: "Anali Mr Alex Simenti."

RIP😭😭😭
19/06/2026

RIP😭😭😭

Dzulo anapanga post yake yomaliza😭😭Rip Lasta💔💔
19/06/2026

Dzulo anapanga post yake yomaliza😭😭
Rip Lasta💔💔

19/06/2026

Jmmy Mtambo
Zabwino 😊

Sad news 💔Mtolankhani wojambula Zinthunzi a Ras Kasengwa watisiya lero.Kasengwa adalemba pa tsamba lake la Facebook dzan...
19/06/2026

Sad news 💔

Mtolankhani wojambula Zinthunzi a Ras Kasengwa watisiya lero.

Kasengwa adalemba pa tsamba lake la Facebook dzana kuti 'Sick' ndipo lero ndipamene tikumva kuti watisiya.

Zambiri tifotokozabe

Mzimu wa Kasengwa ukause mumtendere 💔💔💔

   Komiti yomwe yomwe ikuchita kafukufuku wa ndege yomwe inagwa pa 10 June 2024 ndikupha yemwe anali wachiwiri kwa mtsog...
19/06/2026



Komiti yomwe yomwe ikuchita kafukufuku wa ndege yomwe inagwa pa 10 June 2024 ndikupha yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Saulos Chilima komaso anthu ena asanu ndi atatu ikukumana ndi a Mwayiwawo Polepole omwe pa nthawiyi anali mlembi wa muunduna wa owona za maubale akunja kwa dziko lino.

Wapampando wa komitiyi a Walter Nyamilandu ati undunawu ndiwofunika kupereka umboni potengera kuti ndi omwe umakoza mayendedwe a anthu akuluakulu mdziko.

Address

Blantyre

Telephone

+265996020480

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Daily posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi Daily:

Share