Okonda Ma Blues a Lali Luban Sports Updates

Okonda Ma Blues a Lali Luban Sports Updates Feel free to advertise on this page
Bring any Business we will promote it hereπŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ”₯ at a better price
Call or what's app
0885421436
(1)

26/09/2025

Captain Felix Zulu kuyankhulapo za Game imene akukonzekelayi

25/09/2025

Nyerere kufewa

Afikatu Madolo πŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ™
25/09/2025

Afikatu Madolo πŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ™

Madolowa akufewatu mpaka ndege yawo Yawo Bwana Thom Mpinganjira Ulemu wanuπŸ’™πŸ’™
25/09/2025

Madolowa akufewatu mpaka ndege yawo Yawo Bwana Thom Mpinganjira Ulemu wanuπŸ’™πŸ’™

Wanderers inyamuka leroTimu ya Mighty Wanderers ikunyamuka m'dziko muno lero kupita ku Francistown m'dziko la Botswana l...
25/09/2025

Wanderers inyamuka lero

Timu ya Mighty Wanderers ikunyamuka m'dziko muno lero kupita ku Francistown m'dziko la Botswana lero pomwe akuyembekezeka kukumana ndi timu ya Jwaneng Galaxy mu masewero achibwerenza amu chikho cha CAF Confederations Cup.

Timuyi ikuyembekezeka kugwiritsa ntchito ndege yawoyawo yomwe ithandizire kuti osewera a timuyi asakhale otopa patsogolo pa masewerowa.

Anthu okwana 52 omwe ndi osewera, aphunzitsi ndi akulu-akulu atimuyi akhale nawo pa ulendowu umene akunyamuka nthawi ya 10:30hrds kummawaku.

Osewera ena monga Sama Thierry Tanjong, Mphatso Kamanga komanso Richard Chipuwa omwe akhala ali ovulala akuyembekezeka kukhala nawo pa ulendowu pomwe amachita zokonzekera ndi timuyi.

Manoma anapambana 1-0 mu masewero awo oyamba ndi chigoli cha Felix Zulu pa mphindi 80.

Congratulations AdadiπŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό
24/09/2025

Congratulations AdadiπŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό

Wawa mablues kumeneko πŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό
24/09/2025

Wawa mablues kumeneko πŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ’™πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό

Khaaaaaaa Noma 1-0 inayo Felix zulu
21/09/2025

Khaaaaaaa Noma 1-0 inayo
Felix zulu

πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡
21/09/2025

πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡

mwaithaimaπŸ’™πŸ’™πŸ‘‡
21/09/2025

mwaithaimaπŸ’™πŸ’™πŸ‘‡

A ref nthawi πŸ˜ƒ
21/09/2025

A ref nthawi πŸ˜ƒ

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Okonda Ma Blues a Lali Luban Sports Updates posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Okonda Ma Blues a Lali Luban Sports Updates:

Share