Makilinyombe

Makilinyombe This is Official Page For Makilinyombe
(8)

Congratulations to ndaziona's manager Ken B wazakena ali ndi mwana wa mamuna😘
25/08/2025

Congratulations to ndaziona's manager Ken B wazakena ali ndi mwana wa mamuna😘

25/08/2025

Ndiwe star ngati umaganizira mavuto a kwanu cheers

25/08/2025

Amene amalize kudya nsima pasanadutse 3 minutes apatsidwa K50,000

Mpikisano okudya ukuyamba pompano ku nsika wanjala owina apatsidwa phone komanso ndalama fans yakungana kuno
24/08/2025

Mpikisano okudya ukuyamba pompano ku nsika wanjala owina apatsidwa phone komanso ndalama fans yakungana kuno

23/08/2025

Monga mwa lonjezo K300,000 ija ikugawidwa Monday koma mawa kuli mpikisano okudya owina adzatenga ndalama ndi phone TECNO spark 7 zakozedwa ndi eni ndalama

Our first car zopemphana lift ayi 😂😂
23/08/2025

Our first car zopemphana lift ayi 😂😂

Tilembe mawu anji pa galimoto yi? tikadutsa kwanuko muzidziwa changu😂
22/08/2025

Tilembe mawu anji pa galimoto yi? tikadutsa kwanuko muzidziwa changu😂

First car congratulations to makilinyombe team👏 achina ndaziona, sindi adziyenda chokhala
22/08/2025

First car congratulations to makilinyombe team👏 achina ndaziona, sindi adziyenda chokhala

21/08/2025

Pangani press @ amene abwele pa number 4 akuyankheni pasanadutse 40 seconds owina 5000 kuchoka pa 300,000 ija eni ndalama ali pompano..let's goo!!

20/08/2025

Tatsala ndi 45 minutes kuti 300,000 ija tiyambe kugawa Koma ma vote a 5000 and 2000 akufanana ndiye zitengera vote yanu eni ndalama ali pompano adziona votani zitengera vote

Tiyamba kugawa after 45 minutes mukavota

20/08/2025

Let's vote 300k ija igawidwe motani?

5000 : 60 people
50,000 : 6 people

Titengera ma vote ochuluka

19/08/2025

Ena akuti tigawe 300,000 kwa anthu atatu ayambile business ena akuti bola tigawe 20,000 kwa anthu 15 ena akuti 5000 kwa anthu 60 mukuona kuti tipange bwanji nafe ndalama tangothandizidwa tikufuna kupanga zomwe eni ndalama anena kuti 300,000 ipelekedwe kwa ma fans

Address

Highway
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Makilinyombe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category