Sports Battalion Malawi

Sports Battalion Malawi Giving you the best in Sports in Malawi and in other countries.

13/08/2026

SRFA FINCA Division League 1 Week 11 Results

Saturday, 8th August 2026

- Ekhaya Reserve 3-1 Nyambadwe United
Yusuf Namtunga (Brace
Hestings Malinda
Eric Sadia *

- Liberty FC 0-1 Bullets Reserve
Kondwani Chaula

- The Boyz SFC 4-0 Thondwe FC
Emanuel Nkawa
Yamikani Kazembe
Justice Mahilasi
Frank Mlimanjira

Sunday, 9th August 2026

-Mwanza Stars 2-1 Chilomoni Fc
Chikumbutso Makoloni
Henry Justin
Oscar Nicholas *

- Nchima United 1-2 Ntopwa FC
Chikumbutso Baton (Brace
Grey Dickson

Monday, 10th August 2026

- QPL All stars 5-0 Chiradzulu United
George Chikooka (Haul
Thomas Selemani

- Wanderers Reserve 2-1 Zingwangwa United
Amin Yusuf (Brace
Yohane Mambo *

Thursday 13.08.26

- Chilomoni FC 0-0 Ntopwa FC

13/08/2026

Kodi wayambitsa kuti bola tizingokwera a zimayi omwewa ndi Ndani?

Mr and Mrs Chawinga ndi awatu.Mawu anu ndi otani kwa makolo?
13/08/2026

Mr and Mrs Chawinga ndi awatu.
Mawu anu ndi otani kwa makolo?

13/08/2026

Big shout out to my newest top fans! Chapita OB Rich, Thinzo Degedege Nyirenda, Felix Rhino, Maxwell Scale, Emmanuel Namalima Wa Milanzie, Wiljon Mbewe Francis, Olv Waphe, Paison Oscar Mdoka, John Samson, Allih Mw, HARRIS MATINGA, Bright Chiwenga Chisulo, Kondwani Namaona, Mphatso Teapot, Meke Promise Chakangah, Nsangalatsi Lameck Kalinde, Kumpewu Alfred, Grigory Chiona, VD Makunganya, Mathews Phiri Jabess, Samson Chirwa, Daud Idrissah, Davie Phiri Gabriel, Macdonald Mphako, Gilbert Soko, Jimmy Wa Thonje, Isaac Jham, Grace Dissi, Chiku Steven, Lee K Mittawa, Zaa Chah, Brian Misomali, Sidah Fortune Kamcholo, Emanuel Mathews, Mbwiye Sosten, Barto Barto Mw, Harry Phiri, Drambos Patrick, W***y Thamba, Khoviwah Fi, ɭɭ Manzymecca Mw ɭɭ, Favour W Mayuni Banda, Martin Arex Banda, CLEMZY KAIYA, Mayeso Mayeso, Charly Philip, Skipp Law, Con Chidzalo, Brandinah Bomba, Precious Mbereko

SCORCHERS SPECIALTamverani sports padakali pano pa Litala FM yomwe ili pa 104.8 komanso 105.8Mhz komanso pa internet pa ...
13/08/2026

SCORCHERS SPECIAL

Tamverani sports padakali pano pa Litala FM yomwe ili pa 104.8 komanso 105.8Mhz komanso pa internet pa link iyi

https://sradios.com/Africa/Malawi/Lilongwe/Litala+FM__55085.html

Scorchers yafika mu ndime yotsiriza mu mpikisano WAFCON ndipo ikumana ndi Cameron lamulungu Ndinu okondwa bwanji?

Ikani ndemanga zanu tiwelenga pa wailesi komanso uthenga wanu ku whatsApp 0995571611.

Litala FM is a Chiyao radio station broadcasting from Blantyre, Malawi Litala FM provides African Music, Talk and Variety programs.

Final tikukamuthamangitsa wa Cameroon,, uyu akwadziwenso achina Chawinga naye amangowamva.Sunday wapa stand tikachitenge...
13/08/2026

Final tikukamuthamangitsa wa Cameroon,, uyu akwadziwenso achina Chawinga naye amangowamva.

Sunday wapa stand tikachitenge chinthuchi 🥳🥳

Kwacha bwanji my people Football?Ma Nigeria komanso baneba akuyetsa zabodza angotutumuka aliko.
13/08/2026

Kwacha bwanji my people Football?

Ma Nigeria komanso baneba akuyetsa zabodza angotutumuka aliko.

komatu akanatipatsa Argentina finals chifukwa ma team enawa nde akupepuka kwambiri.NBS bank nde yati iwapatsa ma 7 milli...
12/08/2026

komatu akanatipatsa Argentina finals chifukwa ma team enawa nde akupepuka kwambiri.

NBS bank nde yati iwapatsa ma 7 million aliyese🙌🙌 tiwapatseni malo ku airwing koma

12/08/2026

Are you happy now?

12/08/2026

Tikufuna Morocco mu ndime yotsiriza osati Cameroon ikuchepera kaba.

Address

Ndirande Magalasi Road
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sports Battalion Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category