
24/07/2025
NKHANI YABWINO 📍
Pamene Big2projects tili mkati mwa Fundraising Campaign yomwe cholinga chake ndikupeza ndalama zomangila Center of Innovations yomwe ikhale ikupereka maphunzilo aulere kwa Achinyamata, Tatsitsa mtengo wa book la AGRICULTURE 100 YEARS FROM NOW lomwe Founder wa Big 2 Projects, Blessings Mlelemba adalemba.
Get at only Mk29, 500 from Mk 60,000
Bukuli muli maphunzilo akuya a Climate Smart Agriculture, conservation farming, over 30 crops discussed, organic fertilizer production ( Biochar, Mbeya, fish fertilizer etc) organic poultry farming and feed production.
Center of Innovations ndi malo omwe Big 2 Projects mogwilizana ndi alangizi aboma, LUANAR and NRC graduates ndi ena monga TEVET azizaphunzitsa Achinyamata;
📍 Crop production
📍food processing
📍Entrepreneurship
📍 Carpentry and Tailoring
Achinyamatawa pa mapeto a maphunzilo azipasidwa seed capital, kuwagula zomwe alima komanso kuwapezela misika.
If you want to buy us a book, support the Fundraising or have personal conversation, talk to the founder, Blessings Mlelemba at;
[email protected]
0992 69 84 47
( We also do online trainings, on-ground Consultancy and farm management services, even from zero step at very affordable price)
Fundraising Campaign link
( Detailed center of Innovations campaign and donation platform)
https://docs.google.com/forms/d/e/1FAIpQLSfalaq2bmSawcNUvgXeWytXOSBfScVbY_zlMIZ9DUfqcAqUOg/viewform?usp=dialog