Shire Valley Public Relations

Shire Valley Public Relations Let us help you succeed!

At Shire Valley Public Relations, we provide a market hub for accessing and promoting products, enhancing brand visibility, and sharing valuable information across Malawi.

31/07/2025
MATAMBO VOWS TO COMBAT CR!ME IN CHINGOLABy Beatrice ChabayaGovernment has announced plans to boost security in Chingola ...
21/01/2025

MATAMBO VOWS TO COMBAT CR!ME IN CHINGOLA

By Beatrice Chabaya

Government has announced plans to boost security in Chingola by increasing police presence, allocating K173,000 and over 3,000 liters of diesel for 24/7 patrols, aimed at combating the rising cr!me and vi0lence in the district.

Speaking when he met with the clergy, security personnel, and business leaders recently, Copperbelt Minister Elisha Matambo emphasized that the government would reinforce its commitment to protecting the people of Chingola.

“We are here to reinforce our commitment to protecting the people of Chingola. We understand that security is key to creating a stable environment for businesses to thrive.”

Mr Matambo reassured the people of Chingola that the government ensure that cr!me in the district is combated and not tolerated.

“let me make this very clear, cr!me will not be tolerated. We are determined to confront and deal with cr!minals head-on”, he said.

He praised President Hakainde Hichilema's efforts in fostering peace in the province, saying "thanks to the leadership of our President, the Copperbelt is seeing a restoration of peace. I urge every citizen to remain vigilant. If you see something suspicious, report it without fear."

The minister also commended the Zambia Police Service for their ongoing work, acknowledging the arrests that have already been made, and noted that all ten districts in the Copperbelt are now on high alert to ensure a safe and secure environment for communities.

©️Zambia Reports, 21st January 2025.

Mkulu mukumuona pa chithunzi-yi kwawo ndi ku Mzuzu ndipo zaka za mbuyomu adangochoka mdziko la Malawi kupita ku South Af...
17/01/2025

Mkulu mukumuona pa chithunzi-yi kwawo ndi ku Mzuzu ndipo zaka za mbuyomu adangochoka mdziko la Malawi kupita ku South Africa kuti akasinthe nyengo zake atatenga nthawi zinthu zake osayenda.

Panopa ndi khumutcha. Akukwanitsa kugulitsa anyezi ameneyi zomwe zikumpezetsa ndalama. Akunatumizanso anyezi ku Mzuzu komwe akumagulitsa ma shop akuluakulu.

 .A Patrick Kampira omwe kwawo ndi ku Tsapa m'boma la Chikwawa akuti adzapikisana nawo pa mpando wa nyumba ya malamulo k...
15/01/2025

.

A Patrick Kampira omwe kwawo ndi ku Tsapa m'boma la Chikwawa akuti adzapikisana nawo pa mpando wa nyumba ya malamulo ku mpoto Kwa bomali ngati wa UTM.

Those who have fast finger will be blessed here. Here we go!!!?
17/12/2024

Those who have fast finger will be blessed here. Here we go!!!?

 Kodi mukufuna mutakhala Mlimi wa Nkhuku otsogola?Ngati zili chomwecho, gulani  anapiye awa omwe atha sabata imodzi ndip...
17/12/2024



Kodi mukufuna mutakhala Mlimi wa Nkhuku otsogola?

Ngati zili chomwecho, gulani anapiye awa omwe atha sabata imodzi ndipo alandira kale katemera.

Mmodzi ali pa 2100 kwacha yokha bas

Anapiye-wa akupezeka pa Ngabu m'boma la Chikwawa.

Imbani pa 0990485072

BULLETS YALEPHERA KUTSILIZA CHAKUMWA CHA CASTEL Timu ya FCB Nyansa Big Bullets yalephera kufika mundime yotsiliza ya Cas...
17/12/2024

BULLETS YALEPHERA KUTSILIZA CHAKUMWA CHA CASTEL



Timu ya FCB Nyansa Big Bullets yalephera kufika mundime yotsiliza ya Castel Challenge pomwe yagonja ndi Mzuzu City Hammers lachiwiri pabwalo la Kamuzu munzinda wa Blantyre.

Masewerowa anafanana mphamvu pakutha kwa mphindi 90 ndi nthawi yoonjezera zomwe zapangitsa kuti asewere ma penote kuti apeze odzagwebana ndi Mighty mukuru wanderers yomwe yafika kale mundime yotsiliza itagonjetsa Panthers zigoli zitatu kwa duu.

Ndipo nthawi ya ma penote, Bullets yagoletsa chigoli chimodzi pomwe Hammers yagoletsa zigoli zinayi.

Zateremu Mzuzu City Hammers igwirana pakhosi ndi Mighty Mukuru Wanderers mundime yotsiriza pabwalo la Bingu munzinda wa Lilongwe loweruka sabata ino.

Address

Southern Region
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Shire Valley Public Relations posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category