Moyo Kunyenga

Moyo Kunyenga we don't judge we listen 👂

lero mexico 5 -0 black lebel
11/06/2026

lero mexico 5 -0 black lebel

11/06/2026

lero ndi tsiku labwino Kwa anthu okonda masewero a mpira .... Koma mmmm bola tikwere alendowa .... atsale okha

ndifotokodza za awa
27/04/2026

ndifotokodza za awa

Truth to be told ... sinkhani yokuti anthu oziwika bwino akapalamura nde tiziwamvera chisoni ... khalidwe logonana ndi A...
20/11/2025

Truth to be told ... sinkhani yokuti anthu oziwika bwino akapalamura nde tiziwamvera chisoni ... khalidwe logonana ndi Ana ang'ono ang'ono lachulukira ... what he was preaching it won't stop let him lead by an example ... the punishment he get the more the message spread....

Apolisi omwe amkawonelera anyamata athu akulilongwe akukhapa anthu lero omweo apita kukawakwizinga .....
29/10/2025

Apolisi omwe amkawonelera anyamata athu akulilongwe akukhapa anthu lero omweo apita kukawakwizinga .....

29/10/2025

dzulo amakutumani kuti muzikakhapa anthu lero iwo alumbira dzulo ku parliament akugwira ntchito za boma ... inunso muli mmanja mwaboma ....

  Kadzidzi yemwe anatengeledwa ku polisi ya Nkhotakota m'mawa wa dzulo atapezeka mnyumba ya mkulu wina mmudzi wa Phangwa...
29/10/2025



Kadzidzi yemwe anatengeledwa ku polisi ya Nkhotakota m'mawa wa dzulo atapezeka mnyumba ya mkulu wina mmudzi wa Phangwa watulutsidwa atakhala maola oposa 12 ali wa moyo.

Ena mwa apolisi atsina khutu Times 360 Malawi kuti Kadzidziyo watulutsidwa usiku wathawu ndipo wagwera ku mtsinje wa Chazi omwe uli pafupi ndi polisi ya m'bomali.

Koma mneneri wa polisi ya Nkhotakota, a Paul Malimwe, wauza Times 360 Malawi kuti sangayankhulepo pa nkhaniyi pakadalipano.

Ena mwa anthu anayesera kufika ku mtsinje wa Chazi kuti mwina atha kumuona, koma sizidaphule kanthu.

Malipoti ena akuti eni nyumba yomwe mwapezeka mbalameyi ati sakudziwa ndipo nawo ndiodabwa ngakhale amaganizira kuti mwina munthu wina ndiyemwe wapanga izi.

Kadzidziyo adapezeka mnyumbamo atanyamula uthenga pa kalata ziwiri woti "Undipatse mwamuna wanga" komanso "Iwe Thom nabwera ine tiye tizipita ntchitoyi tikugwilira limodzi tiye ..... SIZINAYENDE MUNTULUTSA BWANJI MESSENGER?

Congrats to her because she made it .... but this is thanks giving ..... kuona kwanga
27/10/2025

Congrats to her because she made it .... but this is thanks giving ..... kuona kwanga

26/10/2025
Vitumbiko mumba dzulo adapangitsa press briefing ataledzela ... kuti akhale ndi confidence. ... stupidity at its best .....
20/09/2025

Vitumbiko mumba dzulo adapangitsa press briefing ataledzela ... kuti akhale ndi confidence. ... stupidity at its best .... kape ka 100

Address

Ndilande
Blantyre
CHICHIRIBLANTYRE3

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Moyo Kunyenga posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share