Martse top fan

Martse top fan Tha freshmans
TOO GHETTO TOO GUTTER

International&Nation covers and Remake music.

Song writer,
Storytelling, Malawian Rapper and manymore
(HIPP-HOPP YA PASSADA YA MARTSE)
πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό

https://audiomack.com/norleo_17

MALUME atasowa NorLeo yemwe Ali ndi Voice yamalume waloleranso kuzipeleka kupitiliza kutumukira ntchito ya Malemu Martse...
19/08/2026

MALUME atasowa NorLeo yemwe Ali ndi Voice yamalume waloleranso kuzipeleka kupitiliza kutumukira ntchito ya Malemu Martse Martin Nkhata. Ndipo pano tikumuthandiza kutulutsa single song yotchedwa "SIIFE OLAKWA"

A MALAWIπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό ngati muja tikulandilira SCOCHEARS mulandileni NorLeo. Ife Martse top fan tikuipempha ku ntundu wa a MALAWI onseπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ™πŸ™. Zikomo

"MALUME ".. Hipp_Hopp ya Martse amaimbira a MALAWI osati zoti atchuke koma kufuna kufumbura mavuto omwe a MALAWI ambiri ...
19/08/2026

"MALUME ".. Hipp_Hopp ya Martse amaimbira a MALAWI osati zoti atchuke koma kufuna kufumbura mavuto omwe a MALAWI ambiri amakumana nawo

Bwana bensam yemwe anali manager wa Martse nthawi imeneyo.. Left person
18/08/2026

Bwana bensam yemwe anali manager wa Martse nthawi imeneyo.. Left person

17/08/2026

MULUNGU amakondwa ndi anthu omwe amayamika nkakang'ono komwe akapezeka.. Let's still support SCOCHEARSπŸ‡²πŸ‡Ό. Tisayakhule kwambir

17/08/2026

Ngati nyimbo zili zomwe zi ine zinganvele, ngati nthano zili zomwezi ine singanvele
Koma "MALUME"

Ndi Nyimbo iti yomwe MARTSE anayamba ndi FREDOKISS??Comment in the section. Don't forget to follow the MARTSE TOP FAN PA...
16/08/2026

Ndi Nyimbo iti yomwe MARTSE anayamba ndi FREDOKISS??

Comment in the section. Don't forget to follow the MARTSE TOP FAN PAGEπŸ™πŸ™πŸ™

Kwangocheratu "inenso ndi Top fan tu ndiye mundiposte ko" koma atsikanaa Martse eeh ndi ovuta kulera Koma tiyamike kuti ...
15/08/2026

Kwangocheratu "inenso ndi Top fan tu ndiye mundiposte ko" koma atsikana
a Martse eeh ndi ovuta kulera
Koma tiyamike kuti Martse anali ndi ma top fan omukonda ndi Ntima onse not only pa Maso pokha ayi. Ngati unali top fan wa Martse follow this page and show us your love by comment
πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡

15/08/2026

Mwadzuka bwanj nonse
πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡Ό
Are you MARTSE TOP FAN?

Management yathu yayamba dongosolo la Nor Leo kuti ayambe kutitumikira ku Music. Tipempha ma top fan nonse pano ndi aliy...
14/08/2026

Management yathu yayamba dongosolo la Nor Leo kuti ayambe kutitumikira ku Music. Tipempha ma top fan nonse pano ndi aliyense kuti mumulandire bwino bwino ndi mwaunyinji Nor Leo pakuti Tonse ndife a MALAWI

Ngati mwasangalala naye comment πŸ‘‡πŸ‘‡πŸ‘‡

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Martse top fan posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share