18/09/2025
Of course we all want to move to another level in life but sometimes we are where we are by God's plan, we are there for protection.
Inde timafunisisa titasuntha kupita Pena komano nthawi zina zimakhala kuti ndi Mulungu amene akufuna tikhale pomwe tilipo kuti titetezeke.