28/04/2025
KODI MUKUZIWA?
Martial Focus
________________________
1: Nsomba za Shark🐋 zinalengedwa zaka 450 million zapitazo mitengo ilipoyi itsanalengedwe .
2 : Kuyakhula ndi mayi anu okuberekani kumachepetsa nkhawa ndipo ubongo umapepuka komanso kumatchotsa Oxytocin mu nthupi la munthu, mawu amayi anu amafanana ndi hug🫂
3: Cholembera 🖊️ Chachikulu pa Dziko lotse chili Ku lndia ......Cholembera chimenechi ndi chotalika 5.5 mitres komanso chimalemera *34.23kg*
4: Mwatsoka mukadzakumana ndi mzukwa otsathawa ayi uyang'aneni mmaso mwake nkenako upatseni moni , ndipo udzakutsiyan chifukwa umaganiza ngati nanunso ndinu mdzukwa💀💀
5 : Mukatseka maso anu ndi mphuno kenako ndikumadya Apples🍎 , anyezi 🧅ndi mbatatesi 🥔 zonse zimakoma mofanana mukayamba kudya
6: Ku United States of America 🇺🇸 kuli bowa wina munthu akadya kamozi samavanso njala moyo wake onse
7 : Mphudzitsi wina otchedwa *Water Lewin* analila kwa 2 days atapuma pa ntchito ( Retirement) , mkuluyu anayamba kulila atangomalidza Kuphunzitsa mphunzilo la Physical Science.
8: Ku Russia kuli mnyamata wina yemwe akuti iyeyo amakhala Ku Mars🪐🪐 asanabadwe pa dziko lino la pansi , Ndipo akuti Ku Mars kumeneku ankapuma mpweya wa Carbon Dioxide okhaokha otsati Oxygen
9 :Nthawi yabwino yowerenga ana a School ndikuyambila 4am mpaka 6am m'banda kucha ubongo umagwila ntchito 100% pomwe 6am to 8pm ubongo umagwila ntchito 50% utsiku umagwila ntchito 25%
10 : Ka chilombo kotchedwa Scorpion🦂🦂 kamakhara 6 days otsapuma komanso 1 year otsadya kanthu ikoka kamadalila light ya dzuwa ndi komwe kamapedzako mphavu
11: Mu Chaka cha 2029 mwala wawukulu kwambili otchedwa *Apophis* udzagwa kuchokela mwamba , koma mwalawu siwudzagunda dziko lapansi anthu pafupifupi 2 billion azawuwona mwalawu
12: Munthu thupi lake limatsitha pakutha kwa zaka 10 zilizonse
13: *Harnaar Kaur* ndi msikana oyamba pa dziko lonse lapansi yemwe alindi ndevu zambili
14 : Ma Condom amagulitsidwa kwambili mwezi wa March ndi June pa d