Magix phone expert

Magix phone expert Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Magix phone expert, Digital creator, Blantyre.
(1)

๐Ÿ“ฑTips & Tricks for Smartphones
โšก Fast help & simple solutions

Kudziwa phone kupotsa momwe mmaidziwira

๐Ÿ” Follow Our Backup Page:
๐Ÿ‘‰ Magix Phone Expert Backup
https://www.facebook.com/profile.php?id=61581569365303

KODI MUNGATANI NGAT PHONE YANU IKUONONGA BUNDLE YOCHULUKA Ngati foni yanu ik*tha Data mwachangu, tsatirani njira izi, ma...
26/08/2026

KODI MUNGATANI NGAT PHONE YANU IKUONONGA BUNDLE YOCHULUKA

Ngati foni yanu ik*tha Data mwachangu, tsatirani njira izi, makamaka pa mafoni a Android ๐Ÿ‘‡

1. Yatsani Data Saver
Iyi ndi njira yabwino kwambiri yomwe imathandiziza k*ti phone isamaononge bundle yochuluka

Momwe mungaysike data saver

Pitani ku Settings

Dinani Network & Internet kapena Connections

Sankhani Data Saver

Yatsani Data Saver

โžก๏ธ Izi zimathandiza kuchepetsa kugwiritsa ntchito Data kwa ma app omwe akugwira ntchito ku background kapena ma app omwe simukuwagwilitsa tchito

2. Letsani ma app kugwiritsa ntchito Data pomwe simukuwagwilisa tchito

IMa app ena amagwiritsa ntchito Data ngakhale simukuwagwiritsa ntchito izitu ndizomweso zimaononga bundle yochuluka ngakhale kt simukuwagwilisa tchito app yo

Kuti muthumise
1 Pitani ku Settings
2 Dinani apps ma phone ena app management

4 Sankhani app yomwe imagwiritsa ntchito Data kwambiri, monga Facebook, Instagram, TikTok kapena YouTube

5 Dinani Mobile data & Wi-Fi

6 Zimitsani Background data

Zambili ndafotokoza mu video link ili mu comment box ๐Ÿ‘‡

kodi zak*thekelani zithu izi ๐Ÿ“ธโœ… Kuloka screen ya phone pogwiritsa ntchito cameraโœ… Kuyatsa Toch pogwiritsa ntchito camera...
23/08/2026

kodi zak*thekelani zithu izi ๐Ÿ“ธ

โœ… Kuloka screen ya phone pogwiritsa ntchito camera
โœ… Kuyatsa Toch pogwiritsa ntchito camera
โœ… Kutsegula Camera pongogwira camera yokha

Ngat video inakuphonyani link ndiika mu comment box

22/08/2026

Zinayambila pa phone FL mobile studio pano zikukula pang'ono pang'ono๐Ÿ˜‚ chiyambi ndichovuta koma big up my brother cheyzar ck

22/08/2026

Thawi yoyang'ana app camera k*ti mujambule zithuzi inatha

Mu video yi ndaonesa zomwe mungapangile k*ti camera ya phone yanu izizinsikila k*ti iuze system ya phone yanuyo k*t ipange zithu izi

Kuyasa toch
Kuthimisa screen
Kusegula app ya camera
Kutenga screen shot

Ndi dzina zambili

Onelani video yi k*ti zabwinozi zisakuphonyeni osaiwala kupanga like comment and share

pazomwe ndakhala ndikuphuzitsa ndi ziti zomwe zikukuvutanibe?
20/08/2026

pazomwe ndakhala ndikuphuzitsa ndi ziti zomwe zikukuvutanibe?

SAMSUNG SYSTEM UPDATESTimaziwa k*ti kupanga update phone kumathandiza phone kukoza ma vuto ena koma thawi zina update yo...
20/08/2026

SAMSUNG SYSTEM UPDATES

Timaziwa k*ti kupanga update phone kumathandiza phone kukoza ma vuto ena koma thawi zina update yo imatha kuyambisaso vuto pa phone yathu

A Samsung atulusa update yama phone omwe imapanga support One UI 8.5, monga awa:

๐Ÿ“ฑ Galaxy A34 5G
๐Ÿ“ฑ Galaxy M34
๐Ÿ“ฑ Galaxy F34
๐Ÿ“ฑ Galaxy A25

ndi ena ambiri, pakadali pano musathamangire kupanga system update.

Pali ma phone ena omwe ukapanga update system, imatha kuyamba vuto la touch screen, mpaka touch kusiya kugwira ntchito bwino.

Kuyesera kusintha screen kapena kupanga flashing sizik*theka k*thesa vutoli chifukwa vuto si touch screen ayi koma system yomwe mwapanga update yo

Vutoli likafika apa limafunika technician wodziwa bwino ntchito yake, kuchosa IC,wa phone yo kenako kuchita programming pogwiritsa ntchito ukadaulo wapadera.

Samsung users omwe muli ndi ma phone amenewa, samalani musapange system update mk*theka mukhoza kukumana ndi vuto limeneli

NOTE:Sima phone ose a Samsung omwe akukumana ndi vuto limeneli.

19/08/2026

Website yabwino kwambiri yomwe mungapangile download ma software apa computer, Mac, komanso apa Android โ€

๐Ÿšจ Palibe chowawa ngati kugula phone ya ngongole! ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ“ฑ๐Ÿ“ฑ Pogula phone ya second-hand, samalani kwambiri! Izi ndimakonda kune...
17/08/2026

๐Ÿšจ Palibe chowawa ngati kugula phone ya ngongole! ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ“ฑ

๐Ÿ“ฑ Pogula phone ya second-hand, samalani kwambiri! Izi ndimakonda kunena pa page lino chifukwa anthu ambiri amandipeza ndi mavuto ngati amenewa.

Zimaphala zopweteka kugula phone ya ndalama zochuluka kungogwilisa tchito kwa thawi yochepa phone ija ndikulokedwa๐Ÿ˜ฅ

Pamenepo umakhala k*ti ndalama zapita ndipo phone siyikugwiranso ntchito. Chomwe chimapweteka kwambiri ndi kuyesa kufufuza munthu amene anakugulitsani, koma osamupeza. ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ’”

๐Ÿค” Nanga tingadziwe bwanji ngati phone yagulidwa pa ngongole?

โ–ถ๏ธ Onani video yomwe ili mu comment box ๐Ÿ‘‡ k*ti mudziwe zomwe muyenera kuyang'ana musanagule phone ya second-hand.

Ngati mwagula phone yogulidwa pangongole pitilizani kulipila phone yo mpaka mumalize ngongoleyo osaflashisa phone yangongole mukathela ku waya๐Ÿ˜…

17/08/2026

Ngakhale ta luza koma ndi angati taonela mpira wa malawi ndi Cameroon pogwilitsa tchito famelack?

16/08/2026

Kt muonele mpira wa Malawi ndi Cameroon satilan video iyi

Osaiwala kupanga follow page lino

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Magix phone expert posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share