
11/08/2025
Kodi ndindani oyenela kumvotela Ife asilamu ?
YANKHO:
Ndime yochoka m'qur'aan: Suurat Al-Mujaadilah (58:22)
لَّا تَجِدُ قَوْمًا يُؤْمِنُونَ بِاللَّهِ وَالْيَوْمِ الْآخِرِ يُوَادُّونَ مَنْ حَادَّ اللَّهَ وَرَسُولَهُ وَلَوْ كَانُوا آبَاءَهُمْ أَوْ أَبْنَاءَهُمْ أَوْ إِخْوَانَهُمْ أَوْ عَشِيرَتَهُمْ ۚ أُولَـٰئِكَ كَتَبَ فِي قُلُوبِهِمُ الْإِيمَانَ وَأَيَّدَهُم بِرُوحٍ مِّنْهُ ۖ وَيُدْخِلُهُمْ جَنَّاتٍ تَجْرِي مِن تَحْتِهَا الْأَنْهَارُ خَالِدِينَ فِيهَا ۚ رَضِيَ اللَّهُ عَنْهُمْ وَرَضُوا عَنْهُ ۚ أُولَـٰئِكَ حِزْبُ اللَّهِ ۚ أَلَا إِنَّ حِزْبَ اللَّهِ هُمُ الْمُفْلِحُونَ ﴿٢٢﴾
22. Supeza anthu okhulupirira mwa Mulungu ndi tsiku lomaliza akukonda Amene akuda Mulungu ndi Mthenga Wake, ngakhale atakhala atate awo, ana Awo abale awo ndi akumtundu wawo; Kwa iwo (Mulungu) wazika Chikhulupiriro (champhamvu) m'mitima Mwawo, ndipo wawalimbikitsa ndi Mphamvu zochokera kwa lye. Ndipo Adzawalowetsa m'minda yomwe pansi Pake pakuyenda mitsinje; adzakhala M'menemo muyaya. Mulungu Adzakondwera nawo ndipo (iwonso) Adzakondwera Naye. lwowa ndi chipani Cha Mulungu. Dziwani kuti Chipani cha Mulungu ndichopambana.