Salim Chazama

Salim Chazama Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Salim Chazama, Digital creator, Blantyre.

For those who would like to sponsor boxing or advertise their products, contact me Salim Chazama on this what's app number
+265991581601 and we are ready to work with any company that wants to support boxing. πŸ‡²πŸ‡Ό

21/08/2026

Jaki walowa gulu lathu wayilongosolaso bwino nkhani. akanakhala enawa akanangozipakapaka kuzikolakola The Jaki Show ineyo ngat commander wa boxing ndakupatsa ma flowers 🌼🌹🌼🌹 jaki osazamupheketsa ayi dolo kwambiri mbiri πŸŒΌπŸŒΌπŸŽ‡πŸŽ†πŸ«‘πŸ«‘

20/08/2026

Master Tchingilayu sadzatheka guys

Bill yanga iyiyi
20/08/2026

Bill yanga iyiyi

πŸ₯Š Ntchito zazikulu za promoterKukonza fight – kusankha tsiku, venue ndi ma fights.Kusaina ma boxer – kukambirana ndi box...
20/08/2026

πŸ₯Š Ntchito zazikulu za promoter

Kukonza fight – kusankha tsiku, venue ndi ma fights.

Kusaina ma boxer – kukambirana ndi boxer/manager za fight ndi purse.

Kulipira ma boxer – malinga ndi contract yomwe yasainidwa.

Kupeza ndalama ndi sponsors – kufunafuna sponsorship, ticket sales ndi ndalama zina za event.

Marketing & advertising – ma poster, social media, press conference, interviews ndi promotion ya fight.

Kukonza venue – ring, lighting, sound system, security, seating ndi zina.

Kukonza weigh-in ndi press conference mogwirizana ndi Board.

Kugwirizana ndi Boxing Control Board kuti ma boxer, medicals, officials ndi fight zonse zikhale approved.

Broadcasting/streaming – kukonza TV, radio kapena livestream ngati ilipo.

Kukonza event yonse mpaka itatha komanso kuonetsetsa kuti anthu omwe ali mu contract alandira zomwe adagwirizana.

⚠️ Koma promoter alibe mphamvu zonse
Promoter sayenera kusankha yekha referee, judges kapena kusintha official result. Izi ziyenera kukhala pansi pa Boxing Control Board/Commission.

Mwachidule:
πŸ‘‰ Promoter amabweretsa ndalama, boxer, venue ndi audience pamodzi kuti fight ichitike.

πŸ‘‰ Control Board imayang'anira kuti fightyo ndi yotetezeka komanso ikuyenda motsatira malamulo.
Salim Chazama

20/08/2026

Miyambo 29:15 ndodo ndichidzudzulo zimapatsa nzeru.

20/08/2026

Belt atsala kapena akwera ndege?? Zonse ndi pa 30

Tonse pano  president wathu ndi uyuyu wa ndewu lonzoe Defector Zimba
20/08/2026

Tonse pano president wathu ndi uyuyu wa ndewu lonzoe Defector Zimba

𝟏𝟎 πƒπšπ²π¬ 𝐓𝐨 𝐆𝐨𝐨𝐨 πŸ₯ŠπŸ‘ŠπŸ‘ŠπŸ‘ŠπŸ”₯πŸ”₯Buy Your advance Ticket motchipa pa Kwenda.co
20/08/2026

𝟏𝟎 πƒπšπ²π¬ 𝐓𝐨 𝐆𝐨𝐨𝐨 πŸ₯ŠπŸ‘ŠπŸ‘ŠπŸ‘ŠπŸ”₯πŸ”₯
Buy Your advance Ticket motchipa pa Kwenda.co

20/08/2026

Guy's Snowden munyanje akupanga mwano ndimusemelatu chinyawu uyu

πŸ₯Š KODI KU BOXING KUMAKHALA PENALTY?Inde, ku boxing kumakhala ma penalty ngati boxer waphwanya malamulo a fight. Penalty ...
19/08/2026

πŸ₯Š KODI KU BOXING KUMAKHALA PENALTY?

Inde, ku boxing kumakhala ma penalty ngati boxer waphwanya malamulo a fight. Penalty si nthawi zonse kukhala ndalama. Referee angapereke warning, kuchotsa point, kapena ngati cholakwacho ndi chachikulu kwambiri, boxer angachotsedwe pa fight (disqualification) imeneyi ndiye penalty yaku boxing..

Zolakwa zomwe zingabweretse penalty ndi monga:
πŸ‘‡
Kumenya kumbuyo kwa mutu
Kumenya pansi pa lamba
Kulumana
Kugwiritsa ntchito mutu kapena zigongono mwadala
Kugwira mdani mopitirira muyeso
Kusamvera malangizo a referee

πŸ‘‰ Choncho, boxer ayenera kudziwa ndi kutsatira malamulo kuti apewe penalty komanso kutaya ma point.

πŸ₯Š BOXING SI KUMENYANA KOKHA β€” NDI SPORT YA MALAMULO, DISCIPLINE NDI RESPECT.

Address

Blantyre

Telephone

+265991581601

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Salim Chazama posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Salim Chazama:

Shortcuts

Share