MBALI Yakuno

MBALI Yakuno MALAWIAN CAPABLE

23/06/2026

MOST DANGEROUS ANIMALS IN ๏ฟฝ AFRICA

Koma Capetown ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ zaonjeza ๐Ÿšจ MZIMBABO  WINA  WABAYIDWA MIPENI KA 10 PA DUMPING SITE YA KU MEYERTON โ€“ WOKAYIKIRIDWA WAMAN...
13/03/2026

Koma Capetown ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ zaonjeza

๐Ÿšจ MZIMBABO WINA WABAYIDWA MIPENI KA 10 PA DUMPING SITE YA KU MEYERTON โ€“ WOKAYIKIRIDWA WAMANGIDWA! ๐Ÿšจ

Mwamuna wazaka 35 wabayidwa mipeni kangapo, kufika ka 10, pafupi ndi Springfield Dumping Site mโ€™mbali mwa msewu wa M61 R59 ku Meyerton, m'mawa kwambiri
Malinga ndi apolisi, mwamuna wina wazaka 27 wamangidwa chifukwa chokayikira kuti ndi amene anachita nkhanza zimenezi. Akuti wokayikiridwayo anapezeka akubisala pafupi ndi malo omwe chochitikacho chinachitikira.
Apolisi awonjezera kuti wokhudzidwayo wapalamulidwa mlandu, ndipo kafukufuku pa nkhaniyi ukupitilira. ๐Ÿ‘ฎโ€โ™‚๏ธ
Nkhaniyi ikupitiriza kufufuzidwa.

10/10/2025

MALAWI ๐ŸŒŸ๐ŸŽ‰๐ŸŒŽ

09/10/2025
12/08/2025

Open

Address

Nacholi
Blantyre
CHILLS

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MBALI Yakuno posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share