20/08/2026
โ ๏ธ SAMSUNG UPDATE WARNING
Timaziwa kuti kupanga update phone kumathandiza phone kukoza ma vuto ena koma thawi zina update yo imatha kuyambisaso vuto pa phone yathu
A Samsung atulusa update yama phone omwe imapanga support One UI 8.5, monga awa:
๐ฑ Galaxy A34 5G
๐ฑ Galaxy M34
๐ฑ Galaxy F34
๐ฑ Galaxy A25
ndi ena ambiri, pakadali pano musathamangire kupanga system update.
Pali ma phone ena omwe ukapanga update system, imatha kuyamba vuto la touch screen, mpaka touch kusiya kugwira ntchito bwino.
Kuyesera kusintha screen kapena kupanga flashing sizikutheka kuthesa vutoli chifukwa vuto si touch screen ayi koma system yomwe mwapanga update yo
Vutoli likafika apa limafunika technician wodziwa bwino ntchito yake, kuchosa IC,wa phone yo kenako kuchita programming pogwiritsa ntchito ukadaulo wapadera.
โ ๏ธ Choncho pakadali pano, Samsung users omwe muli ndi ma phone amenewa, samalani musanapange system update.