SKC Pride mw

SKC Pride mw The Vision Didn't End πŸ‡²πŸ‡Ό
We Continue ✊
Inspired by the Legacy of Dr Saulos Klaus Chilima
Leadership | Reality | A Better Malawi
πŸ’¬ Real voices.

Real conversations

15/07/2026

"Ukadzaona anthu akumenyana, wina nkuyamba kuluma, dziwani kuti olumayo wataniii...?? "

Ikamatha nkhani iyiyi 2030 kudzapikitsana zipani ziwiri basi Mighty UTM ndi DPP chifukwa MCP the Terrorist party ikhala ...
15/07/2026

Ikamatha nkhani iyiyi 2030 kudzapikitsana zipani ziwiri basi Mighty UTM ndi DPP chifukwa MCP the Terrorist party ikhala kuti yatha..the End of Chikangawa party

14/07/2026

Nanga chimene anakanizila kuti akubanja asaone nkhope ndi chani? angopita akafukule mandawo kenako akapange DNA, period...!

14/07/2026

Mimba zina phwelaphwela..Kumaliopa mawa
Nanga ichi mchiyani?

continue ✊

Ka m'dala kakafupika zoona kupeleka mzake eish...munasewera game yofoila amphwanga  continue ✊
14/07/2026

Ka m'dala kakafupika zoona kupeleka mzake eish...munasewera game yofoila amphwanga

continue ✊

13/07/2026

Dear Biyeni πŸ’”
Onena analipo koma amalawi ukhutukumve

continue ✊

Mimba zinaphwela phwela ... Ilindi dzikotu mukaona ngati mukawapha anthu aja mukhala mu mtendere? Justice wanna be serve...
13/07/2026

Mimba zinaphwela phwela ... Ilindi dzikotu mukaona ngati mukawapha anthu aja mukhala mu mtendere? Justice wanna be served very soon

continue ✊

Musanamizidwe 2030 mwinaso kwatalika   and the Mighty   ikutenga chinthuchi.Iyi ndi UTM NEC meeting imene ikuchitikila k...
13/07/2026

Musanamizidwe 2030 mwinaso kwatalika and the Mighty ikutenga chinthuchi.
Iyi ndi UTM NEC meeting imene ikuchitikila ku UTM Headquarters mu Area 10 ku Lilongwe

Vision Didn't End ✊

13/07/2026

" Mkamwini wa mwano amampatsa munda wa pakhomo kuti mbuzi zizimudyera "

Team SKC Pride mw Kodi K.K.K akutanthauzanji? Ndichitseni umbuli chonde  continue ✊
13/07/2026

Team SKC Pride mw Kodi K.K.K akutanthauzanji? Ndichitseni umbuli chonde

continue ✊

Address

Malawi
Blantyre
0001

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when SKC Pride mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share