TIMVE NAWO

TIMVE NAWO your number one trusted media/news company

01/04/2026

New Fuel Prices:
Petrol K6,672 Per Litre
Diesel K6,687 Per Litre
#

03/03/2026

Apha

Breaking News  High court yakana pempho la Malawi Electoral commission kukana kuchoka Ku Lilongwe  kusamuka kupita Ku Bl...
26/02/2026

Breaking News

High court yakana pempho la Malawi Electoral commission kukana kuchoka Ku Lilongwe kusamuka kupita Ku Blantyre

President APM analamula Bungweli kuti Head office ibwelele Ku Blantyre koma MEC Inakana ndikupita ku court kuti ma judge alowelelepo akhale chishango chao koma ma judge lero akana ati ai tsatilani zimene Mwalamulidwa mwachedwa kubweka kuno.

22/02/2026

Nyasulu anaipulumutsa FCB

 Sipikala wa Nyumba ya Malamulo a Sameer Suleman ati munthu wina yemwe sakudziwika wagwetsa chithumwa m'nyumbayi.A Sulem...
20/02/2026



Sipikala wa Nyumba ya Malamulo a Sameer Suleman ati munthu wina yemwe sakudziwika wagwetsa chithumwa m'nyumbayi.

A Suleman apempha munthu yemwe wagwetsa chinthuchi kuti adzachitole.

Iwo ati aphungu asamabweretse zinthu zopuma chotere ku Nyumba ya Malamulo.

M'munsimu ndi zithunzi za chithumwa chomwe tachijambula kunja kwa nyumbayo komanso pa malo omwe chinapezeka

16/02/2026

Ndampeza Bongie

15/02/2026

Mtendere by Gibo pearson

13/02/2026

Ngoz

07/02/2026
30/01/2026

Mwinadi mwini wake wa nyimbo ndi uyuyu

25/01/2026

Ada awawa ndi dolo ndipo 35mita yapita koyenera eee🔥🔥

Address

Pvt Bag 68
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when TIMVE NAWO posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share