Iwe Wagwan

Iwe Wagwan Ghetto Muzik rise up

27/10/2022

NYAMATA WINA YEMWE ANAMWALIRA ZAKA 20 ZAPITAZO WAPEZEKA WAMOYO.

Nyamata wina yemwe anamwalira zaka makumi awili zapitazo ku Thekelani mudzi mwa Ndongo T/A Nsabwe wapezeka wa moyo ku Zalewa muboma la Blantyre.

Mfumu yayikulu Ndongo yasikimiza zankhaniyi kuti nyamatayi yemwe dzina lake ndi Paulo Phaiva anamwalira muchaka cha 2002 nthawi yomwe anali ndizaka 10 zakubadwa.

Nyamatayi atamwalira anthu analira maliro ndikukamiyika m'manda.

Masiku apitawa mzimayi wina wokhala ku Zalewa muboma la Blantyre atapita kotunga madzi anakumana ndinyamatayi ali chogonele ndinso akuwoneka ofowoka. Ngakhale ankalephela kuyankhula zomveka nyamatayi anakwanisa kutchula mudzi wakwawo ndi dzina la mayi ake.

Mzimayiyu atapita ndinyamatayi kumudzi komwe amatchula mayi ake ndi achibale anali odabwa kuwona kuti mwana wawo yemwe anamwalira ndikuyikidwa m'manda zaka 20 zapitazo wapezeka wamoyo.

Atamuyang'anisisa mayi ake anakhulupilira zamwanayo kamba kachipewa chomwe anamugulira ali ndi zaka 10 ndipo mosakhalisa anamulandila ndikumufusa zakomwe anali.

Asing'anga ena anawuza achibale kuti mwanayo anasandusidwa chabe ndondotcha ndimpondamatiki wina koma wabwelelaso ku umoyo wake kamba koti zizimba zomwe mpondamatikiyo anagwilitsa ntchito zasuluka.

Pakanali pano nyamatayi ali ndizaka 30 ndipo watha zaka 20 makolo ake akuyesa kuti anamwalira osaziwa kuti anangophedwa mumasenga ndipo thupi lake linachosedwa kumakagwilitsidwa ntchito ngati ndondotcha

Follow Page Mr Screenshot Mw 🙏🏽

17/10/2022

Like the page

17/10/2022

Kumenya jugwetsa

#22

Moto wawo

10/10/2022

Ka Chibwezi kanuko kasamakunamizeni kuti kamakhoza bwino mu standard 1 muja
Ingokawuzani kawelenge mawu awa

GWA GWE GWI GWO GWU
kapena
NGWA NGWE NGWI NGWO NGWU
asamakunamizen

Like page and shere to get more fany post

09/10/2022

Tivelele ma piano & -Boss

Mamuna wasiliyasi uja Wapezeka
09/10/2022

Mamuna wasiliyasi uja
Wapezeka

Kasamben Bambo
09/10/2022

Kasamben Bambo

Address

Ghetto Yard
Chikwawa
MALAWIHITMUSIC

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Iwe Wagwan posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category