SG Creation

SG Creation UNVEILING IMAGINATION ✨

GOOD MORNING....πŸ€—HAPPYSUNDAY
10/08/2025

GOOD MORNING....πŸ€—
HAPPYSUNDAY

Palibe kugona 🚨
14/12/2024

Palibe kugona 🚨

Tuno remains Tuno,Morning everyone πŸ˜‚πŸ˜‚
14/12/2024

Tuno remains Tuno,
Morning everyone πŸ˜‚πŸ˜‚

December 😎
01/12/2024

December 😎

  Atsikana azaka zosapyola 15 zakubadwa ku Mchinji, omwe amagwira ntchito zoyendayenda adandaula ndikusowa Kwa kulera wa...
01/12/2024



Atsikana azaka zosapyola 15 zakubadwa ku Mchinji, omwe amagwira ntchito zoyendayenda adandaula ndikusowa Kwa kulera wapangozi (Emergency pills) kwa mwezi tsopano mzipatala za bomali.

Ena mwa atsikanawa atiuza kuti iwo amagwiritsa ntchito mankhwalawa kamba koti abambo ambiri omwe akumakhalira nawo malo amodzi akukana kulipira ndalama zochuluka akagwilisa ntchito njira zozitetezela.

"Yoziteteza ndi 3000 ena amatipasa 1500 pomwe osaziteteza ndi 4500" watelo m'modzi wa atsikanawa.

M'mawu ake mkulu wa bungwe logwira ntchito ndi achinyamata la CISE Malawi, Davis Damson wati nthawi yakwana tsopano kuti atsikana omwe akuchita m'chitidwewu auzidwe mwachindunji zakuipa kwake.

"Zithuzi za matenda opasilana anthu akakhala malo amodzi mosaziteteza zitha kuthandizira kuti anthuwa azisankha njira yozitetezela kumatenda komaso mimba" Atelo a Damson.

Mankhwala a Emergency pills omwe ntchito yake ndi kuteteza mai kuti asatenge pakati akagonana ndi bambo osaziteteza koma sateteza kumatenda opasilana pogonana.

Olemba: Patrick Nditi Nyirenda.

30/11/2024

Gwamba zatheka basi sinthan DPπŸ₯Ί

Taking orders!
11/11/2024

Taking orders!

10/11/2024

AMALAWI OMENYA MPIRA WAMIYENDO MULIPO??

24/10/2024

COSOMA OSAMUGANIZILAKO HABAKUK πŸ™„πŸ™Œ

Address

Chitipa

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when SG Creation posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to SG Creation:

Share