Ganic Francis Cheyo

Ganic Francis Cheyo Digital creator
(3)

Take a moment to explore your professional dashboard and discover new opportunities.
22/09/2025

Take a moment to explore your professional dashboard and discover new opportunities.

22/09/2025

Good morning, everyone! Let's come together to celebrate the outstanding work of these innovative content creators: Caroline Kay, Phio Wa August, CALEB, Caleb, Griness Kuyere, Chicco Matias, Charity Chisi Jasper, Mama Princess Lifestyle, Walinase Mike Chigodo Phiri, Ellen Make Bule, Mercy R Chisambiro, Susan Chilomoni, Mphatso Muliya, Mary Wa Leonard, Brown sugars dream, MRS CHA, Chidzukkulu cha Anaphiri, Chirwa A Leah, Caroline Mercy Stewart, Barbara Mai Wa MaBoys, Louy Cee TV, Abdul Chim'z Chinyama, Ñëwtœn.

22/09/2025

22/09/2025

🤭🤭🤭🤭🤭

22/09/2025

Ubwino wake APM ananeratu za izi

20/09/2025

Follow Ñëwtœn afike 1k followers

ku Cameroon, mwana wa president Biya,  yemwe dzina lake ndi Brenda Biya, analowa live pa tiktok .ndipo iye atalowa live ...
19/09/2025

ku Cameroon, mwana wa president Biya, yemwe dzina lake ndi Brenda Biya, analowa live pa tiktok .

ndipo iye atalowa live yake, Brenda anapempha anthu kuti asavotelenso bambo ake, amene akhala akulamulira kwa dzaka zokwana 43.

Iye wati abambo akewa ndi chipani chawo ndichomwe chadzetsa umphawi
Dziko la Cameroon.

dzikoro likuyembekezeka kuchititsa ma elections awo mwezi wa October chaka chomwechino cha 2025.

19/09/2025

Tili mu nthawi ya zisankho

19/09/2025
19/09/2025



Wapampando wa bungwe la MEC a Annabel Mtalimanja ati bungweli liyamba masana ano kugwira ntchito yowona kuti wapambana ndi ndani pa chisankho chomwe changochitika kumene m'dziko muno.

A Mtalimanja ayankhula izi lero ku BICC ku Lilongwe pomwe amalandira mapepala omwe azigwiritsa ntchito polowetsa zotsatira za opambana pa chisankho cha mtsogoleri wa dziko, phungu komanso khansala.

Katunduyu amasungidwa ku malo wosungira katundu a MEC ndipo watsegulidwa pa maso pa oyimira zipani, atolankhani komanso oyang'anira chisankho ochokera mabungwe osiyanasiyana

*📘MK NEWS UPDATE 🖊️*

Ndi zoona izi koma 🤔🤔🤔
19/09/2025

Ndi zoona izi koma 🤔🤔🤔

19/09/2025

Kwavuta Tally Center pomwe gulu lochuluka likuyimba nyimbo yoti.

"Dziko tinakupasa walephera wekha."
"Dziko tinakupasa walephera wekha."

Address

Chitipa

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Sunday 09:00 - 17:00

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ganic Francis Cheyo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share