
23/02/2025
Ndiye mwati
Kodi a Onesimus akoma chotani? Kodi mwaimva? Zamalaulotu🙌🏻
Mkadzi wa ku Botswana dzina lake Kessyjan tikunena pano wauyamba ulendo obwera ku Malawi waikwera Ndege akufuna azizamuonela African Chiponde yo pafupi
Phunziro pa nkhaniyi : sitingakulese kuti ubwere koma pomwe wafika Malawi panopa uzathawako wekha zambiri uzazionera komkuno