Kamtunda

Kamtunda Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kamtunda, Digital creator, Dedza.

22/08/2026

soya pieces amatiyimila zolandila zilizonse salephera kukhalapo😇

NKHANI YOPATSA CHIDWIPolice ya kanengo ku Lilongwe yamanga Bambo Harold Zimba ndi Mphatso Manyowa pamulandu osowetsa kat...
16/08/2026

NKHANI YOPATSA CHIDWI
Police ya kanengo ku Lilongwe yamanga Bambo Harold Zimba ndi Mphatso Manyowa pamulandu osowetsa katundu wa company ya Zomatira Products okwana 10 million.

Harold amagwira ntchito ku Zomatira ngati driver pamene Mphatso amagwira ngati wa security.

Awiri wa anapanga dinkamu yomatulutsa Juice Flavours kubera kampani yo ndipo akhala akupanga zimenezi kwa miyezi iwiri.

Ndiye Harold anamulonjeza Mphatso kuti akapanga izi amukwatira zomwe samapanga kufikila mtsikana yo anakangoying'alura basi kuyiwala kuti nayenso ndiye kuti akagwidwa nawo

14/08/2026

mamuna wabwino sungamupeze ali single, timachita kulanda🤗🤗. Good night

14/08/2026

kalekalelo mkazi amachita kutomeredwa🤭 koma pano kuli phwanyaphwanya mpira wa akaidi🤣🙌🙌🙌

13/08/2026

Mtembo kuyenda nawo panjinga😭😭😭

Malawi Vs Algeria 🤗🤗All the best faith Chimzimu ( our own goal keeper) lero Takwera Malawi mmwanthawi zonse😇😇
12/08/2026

Malawi Vs Algeria 🤗🤗
All the best faith Chimzimu ( our own goal keeper) lero Takwera Malawi mmwanthawi zonse😇😇

May your souls  rest in peace 💔💔😭
08/08/2026

May your souls rest in peace 💔💔😭

Pepa Wonder Msiska. Ndizopweteka kwambiri 🙄🙄
08/08/2026

Pepa Wonder Msiska. Ndizopweteka kwambiri 🙄🙄

08/08/2026

Very sad😭😭😭😭😭BRIAN BANDA

Rest in peace🙄
08/08/2026

Rest in peace🙄

Address

Dedza

Telephone

+265881491710

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kamtunda posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Kamtunda:

Shortcuts

Share