Jeamson Joy Kalimba

Jeamson Joy Kalimba Radio Alinafe and Mtunthama Radio Station

04/04/2024
31/05/2023

Mlenje amakhala chete pamkumano wa aSodzi.

😂😂😂
Mlenje kudzichepetsa.

.com

28/05/2023

[28/05 09:17] Jeamson Joe Kalimba🤓: One of the prospective to be members of parliament in 2025 elections for Kasungu Municipality Constituency, Wisdom Chimgwede has encouraged people from Kasungu Municipality to use the rubbish bins properly, which has been planted by him in Kasungu Market, where people can throw their rubbish.

Chimgwede said this on Saturday, where he went to Kasungu Market for planting the rubbish bins.

According to Chimgwede, the drums which are using as the rubbish bins, are being bought in the same Kasungu Market, as the one way of empowering people within Kasungu Municipality Constituency.

*Chimgwede spoke to Our Reporter Jeamson Joy Kalimba*

*Insert Chimgwede ENG*
....................

M'modzi mwa anthu omwe akufuna kudzayimira nawo ngati phungu wa manisipalite ya Kasungu, muzisankho zamchaka cha 2025, a Wisdom Chimgwede, alimbikitsa anthu amum'derali kuti agwiritse ntchito bwino malo otayiramo zinyalala omwe iye wakhazikitsa mu nsika wa Kasungu, kuti anthu adzitha kutayiramo zinyalala.

A Chimgwede ayankhula izi loweruka pomwe amakhazikitsa malo otayiramo zinyalawa, mu nsika wa Kasungu.

Malingana ndi a Chimgwede, zinthu zomwe akugwiritsa ntchitozi, zikumagulidwa mu nsika omwewu wa Kasungu ngati njira imodzi yotukula anthu ozungulira mderali.

*A Chimgwede adalankhulana ndi Mtola nkhani wathu Jeamson Joy Kalimba*

*Insert Chimgwede CHI*..........................................
[28/05 09:25] Jeamson Joe Kalimba🤓: .

M'modzi mwa anthu omwe akufuna kudzayimira nawo ngati phungu wa manisipalite ya Kasungu, muzisankho zamchaka cha 2025, a Wisdom Chimgwede, alimbikitsa anthu amum'derali kuti agwiritse ntchito bwino malo otayiramo zinyalala omwe iye wakhazikitsa mu nsika wa Kasungu, kuti anthu adzitha kutayiramo zinyalala.

A Chimgwede ayankhula izi loweruka pomwe amakhazikitsa malo otayiramo zinyalawa, mu nsika wa Kasungu.

Malingana ndi a Chimgwede, zinthu zomwe akugwiritsa ntchitozi, zikumagulidwa mu nsika omwewu wa Kasungu nga

04/05/2023

Mlenje akaona kuti sakuphako ngakhale kalulu m'modzi, amaganiza kwambiri kuti atani mpaka apheko mbawala yokha 😉

Mlenje adzikhala oganiza

09/04/2023

Ma fanz a Arsenal dzanja 💹

Time⌚
09/04/2023

Time⌚

08/04/2023
23/03/2023

Your funniest and best Radio Presenter Jeamson Joe Kalimba ,(Akatundu)very soon will be back OnAir

Address

Karonga

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Jeamson Joy Kalimba posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Jeamson Joy Kalimba:

Share