Zokonda amai macheza

Zokonda amai macheza ticheze amai Kwinaku Tikupanga Ubale Popatsana Mon,kuphuzitsana Maphikidwe,kayendetse Ka Mabusiness Osiyanasiyana Kt Amai Mukhale Ndmoyo Ozidalila.

10/03/2025

Bola ine chabwin ndimalemba zotukwana mesa? KOMA iwe umatamba komaso ndiwe hula πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Chonde usandiweruze uvekere umudziwe Mulungu, aaaa Mulungu ukuona ngat ndiwakwanu

10/03/2025

Mukafika panyumba kumasiyako mafoniwo ndikumacheza mutatsamila osati wina pafoni winaso pafoni

10/03/2025

Banja limakoma ndi kunyengana osangoti bola mzangayu akudya mgayiwa πŸ˜‚πŸ˜‚

10/03/2025

Share and like kuti zokoma zisakuphonyeniπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

02/03/2025

Kumenyedwaa timenyedwe koma mbwanda tipatse azimayi kuchipinda kuja ndikothetsera mikangano

Usakanize nyemba poti wamenyedwa kumeneko ndkudendekera banja
Litha kukupulumuka πŸ˜‚πŸ˜‚

25/02/2025

Tive m'mene ungayitanile mamuna wako kuti akadye nsima
After kumenyedya
Makofi πŸ˜‚πŸ˜‚
Tione ma wife matirials πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

11/02/2025

Big shout out to my newest top fans! Lucy Debritty Banda, Francis Chibisa, Lucia Ongan, Pemphero Captain, Evireen Samson, Vaishiwali Y Yakobe, Shantel Mpira, Maggie Sinkhala, Memz Gunundu, Linnly Jackson, Lucia Msampha, Eliza Munkondya Elisco Msasco, Tryness Nyasulu, Dorica Wa Liwonde, Jean Jelii Hara, Roseline D Matekenya, Alice Kumbemba, Sylvia Chiwato, Gloria Mwale Njiwa, Rhoda Matipa, Nellie Bridge, Chitha Ephridah, Hildah Kalanje, Charity Ntapasya, Mirrium Kwapule, Kira Pindan, Tamie Zembera, Thocco Mbewe, Memori Saka, Cathreen Kettie Wa Justin, Jean Jivah, Getrude Chisambi, Patricia Longwe, Rita Nyirenda, Cindrella Mvula, Phylis Kamoto, Edina Maseko well come all πŸ™πŸ™

11/02/2025

Help me

Kodi kupanda kupita kuchipatala,
Ndingadziwe bwanji kuti ndili ndi mimba?
Podziyeza ndekha

Ndimvekeni chigoba

09/01/2025

Big shout out to my new rising fans! Jude S Cobra, Lucy Dorothy Mkamanga

09/01/2025

Chinaso chomwe chimasunga banja

utha kukhala wa ulemu' utha kukhala katundu kunkhan yakuchipnda koma mamuna atha kukusiyanibe ndikumapita kunja kamba koti simutha kuphika.

Amuna amafuna kudya zakudya zophikidwa bwino komaso zopatsa mudyo
Ndipo ngati chakudya chanu mayi mumangophika ngati waphika ndimwana chosecho zoziyenereza pophika zilipompo
Ndithu mamuna ameneyo akadzangoti wakalawa zina kaya ndikwazake kaya ku resrant chilakolako chachakudya chanucho chidza choka
Zikadzangotero ndi
ngoz

Mphuzilani kuphika bwino banja lizinjoya ndichakudya chanu azimayi chakudya chikamakhars chakudya chimakhalaso kondaine

Chifukwa mamuna komwe angayende amangoganiza za inu komaso chakudya chomwe mumamukozera

Address

Kasungu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zokonda amai macheza posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category