Ndi Chifukwa Chani Brands

Ndi Chifukwa Chani Brands Media Company
(1)

Kodi ndinu Actor, Actress kapena ndi khumbo lanu mutakhala Actor or Actress ?Ife a Team Ndi Chifukwa Chani (TNCC) timaku...
16/08/2025

Kodi ndinu Actor, Actress kapena ndi khumbo lanu mutakhala Actor or Actress ?

Ife a Team Ndi Chifukwa Chani (TNCC) timakumana Loweluka ndi la Mulungu lililonse nthawi ya 2 koloko Masana ku Area 21 mu M'zinda wa Lilongwe.

Muli olandilidwa ✋

C / W : 0884987221 - 0994689540

U T H E N G A   S U L E M E L ATeam Ndi Chifukwa Chani (TNCC) brings you a Trip to Salima 🤸Ku Madzi kwatheka 🔥
12/08/2025

U T H E N G A S U L E M E L A

Team Ndi Chifukwa Chani (TNCC) brings you a Trip to Salima 🤸

Ku Madzi kwatheka 🔥

07/08/2025
06/08/2025
02/08/2025
02/08/2025
31/07/2025

KULENGEZA KOYAMBA

Team Ndi Chifukwa Chani Ikubwera ku Blantyre ndi Futali Party Phase 2 komwe kukakhaleso kachakudya kokoma, M'godo osaiwalaso Chakumwa chathuchathu Thobwa lamwera.

Date : 07th September, 2025
Registration : K5000
Venue : Grace of Abba Arena ( Machinjili Area 7B)

For sponsorship, partnership or registration..
C / W : 0884987221 - 0994689540

31/07/2025
31/07/2025
28/07/2025

FUTALI PARTY - BLANTYRE CHAPTER

Uku kokha sikobwela mutadya kanthu kalikonse. Madyo ali uku ndi aja okamba Nkhani kumapeto 🤸

Venue : Grace of Abba Arena (Machinjili, Area 7B)
Date : 7th September, 2025

Let's spread the News ✊

26/07/2025
24/07/2025

KAPHIKIDWE A SIMA KOMA YOSALIRA KUKANDILA

Choyamba telekani Mpoto wanu wa Sima pa Moto mutayeza bwino kachulukidwe kake ka Nthalo molingana ndi anthu omwe atenge nawo Gawo polemekeza zintchito za Ufa.

Ipatseni nthawi mpaka madzi abwate. Akabwata thilanimo Ufa okwanila bwino, osatakasa kapena kuyamba kutchakula ai.

Ivindikileni kuti Ufa uja olowelere mwabata ndi Madzi obwatika bwino. Pakatha Mphindi zochepa ivundukuleni ndikuyamba kutchakula kwinaku mukuthila Ufa kosalekeza malingana ndi Grade ya kaumidwe ka Sima komwe mumakonda.

Mukamaliza kutchakula kuti yathyakuka bwino, osaphula kaye.. Ivindikileni kwa Mphindi zinai kenako ndikuphula. Apatu imachita kufuka Utsi kuti Zweeeeee !

Basitu mukatero mwamaliza Masewela, zili ndi inuno kuwomola kapena kukhuthula.

Zikomo.

Address

Area 23
Kasungu

Telephone

+265884987221

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ndi Chifukwa Chani Brands posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Ndi Chifukwa Chani Brands:

Share

Category