HOHO TV

HOHO TV Home of entertainment 🌏📺📸
KASUNGU

Hit us on wap 0993836869

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Emmanuel Nhlane, Iryn Ziba Chunga, Sam Kamanga, Bongololo...
04/09/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Emmanuel Nhlane, Iryn Ziba Chunga, Sam Kamanga, Bongololo McMillan Gondwe, Femmie Mhango, Gezire Nhane, Fortune Chabwela, Anastesia Banda, Ro Nah, Josep Kasauke, Cecilia Chirwa, Violet B Kaunda, Molley Highland, Francisco Phiri, Vasco Nyama, Chanta Ome, Francis Chilimanthembwe, Levy Shama, Kenry Gwaza, Samuel Nhlane Banda, Mbappe Mw, Esmy Kamanga, Tazvivinga Tafadzwa, Jerónimo De Moses, Hamid Irani, Mbeumo Morfat, Yacobo Maico, Gïft J Båndā, Notth Mathews, Hydrá Zäyàh, Fazal Muhammad, Adm Oumar Hassan, Masud Mia, Fu Nny, MrCHOCO LATE あ

 Miss Malawi Thandie Chisi wati ali ndi mafunso ochuluka pa zifukwa zomwe oyendetsa mpikisano wa Miss Malawi atulutsira ...
04/09/2026


Miss Malawi Thandie Chisi wati ali ndi mafunso ochuluka pa zifukwa zomwe oyendetsa mpikisano wa Miss Malawi atulutsira email yomwe adawalembera miyezi iwiri yapitayo, yowafotokozera ganizo lake loti sapita ku mpikisano wa Miss Universe.

Poyankhula nafe kudzera pa lamya Chisi wati akukhulupilira kuti oyendetsa Miss Malawi achitira dala pofuna kugwilitsa ntchito dzina lake pa (propaganda) potengera ndi momwe mpikisano wa Miss World ukuyendera ku Vietnam.

Iye wati atapambana mpikisano wa Miss Malawi adawuzidwa kuti adzamuchitira chilichonse ndikumutumiza kukayimira dziko lino ku mpikisano wa Miss Supranational. Koma izi akuti zinayamba kusintha pomwe akuti adamuuza zoti akongole 7-million-kwacha yoti ithandizire kupeza chiphanso chokatenga nawo mbali pa mpikisanowu, ndipo iwo adzabweza mtsogolo.

Iye wati izi zimachitika pa nthawinso yomwe a Miss Malawi-wa amawuza anthu omwe adawagwilira ntchito kuti Thandie ndiye awalipire. Iye watsindikanso kunena kuti a Miss Malawi ali ndi ndalama zake zoti amulipire, zomwe anagwilira ntchito atasayina mgwilizano ndi kampani ina. Iye watinso, pa ndalama ya 50 million kwacha yomwe amayenera kulandira, sadalandire gawo lonse lomwe adamulonjeza (koma watsimikiza kuti adalandira 30 million kwacha).

Poyankhapo mneneri wa Miss Malawi Stephen Mdala watsutsa zomwe wayankhula Thandie Chisi ponena kuti, sadamuuze kuti akakongole ndalama yogulira chiphanso chopitira ku Miss Supranational, koma adamuza kuti athandizire pa ntchito yopeza ndalama. Iye watinso, Miss Malawi inamupatsa Thandie ndalama zake zonse 30 million Kwacha zomwe amayenera kulandira, komanso zomwe anagwilira ntchito.
(by Innocent Kumchedwa – Lilongwe:09/04/26)

04/09/2026

😂 😂 😂

Ndiye ku madness kuli zigawenga izi eeeee ku zepula kokha palineso wina inuyo mkuti bwanj za mys awa🤔📺Continue following...
04/09/2026

Ndiye ku madness kuli zigawenga izi eeeee ku zepula kokha palineso wina inuyo mkuti bwanj za mys awa🤔📺

Continue following HOHO TV for more information

04/09/2026

😂 😂 😂 Utakhala wina bwezi wa ponya mkazi wako ngt addmin waku Øp Ñđåwä

04/09/2026

Iyiyi yokha eti mmmh afana ceez ulemu wanu....

Opanda Ambuye kulibe chouenda kma ambuye ndioneni🤲🤲🤲

Get ready fo bang ❤️‍🩹😍

 Kampani ya msangulutso ku Kasungu ya HoHo Magic Sounds, yati kupeleka mwayi ndi mpata kuti oyimba omwe ayamba kumene az...
03/09/2026



Kampani ya msangulutso ku Kasungu ya HoHo Magic Sounds, yati kupeleka mwayi ndi mpata kuti oyimba omwe ayamba kumene azionetsa luso lawo, kuli ndi kuthekera kotukula luso la oyimbawa komanso kuwalumikizitsa ndi anthu ena omwe akhonza kuwathandiza.

Poyankhula ndi olemba nkhani lero, mkulu wa kampaniyi a Suzgo Nhlane, wati akonza mwambo wa ulele omwe uchitike Loweruka likudzali masana pa bwalo la zamasewero la sukulu ya pulayimale ya boma komwe oyimba osiyanasiyana akaonetse luso lawo.

Malingana ndi a Nhlane, kudzera ku mwambo wa Reignition Kasungu Wake Up, akufuna kupeleka zochita kwa achinyamata omwe nthawi zambiri amasowa zochita koma luso ali nalo ndipo apempha anthu kuti akaonelele.

Mwambowu ubweletsa pamodzi oyimba monga Lil Kelz, Casino, Nester, Followman, Wespar, Maleek Mw, Queen Nefa, Wongie ZBL ndi Kasungu CCAP Praise Team.

(by Wilson Allan Phiri-Kasungu 09/01/26)

03/09/2026

Ndye kuli ichi chinakomesa day ija ya chikwani munayiona bwanj

01/09/2026

Ku Malawi 🇲🇼 khani ya sports yokha amaonesesa kt ngati akuza mpila ku saport yokha sizitheka inu mukuona bwanji pa khani ya saport amalawi

Ka muthu aka kokha ndye kanabwela kuzakhlgalaa kuno ku Malawi 🇲🇼 nyimbo zokha ndye kakuzimphweteka🙌🙌🙌😍😘
01/09/2026

Ka muthu aka kokha ndye kanabwela kuzakhlgalaa kuno ku Malawi 🇲🇼 nyimbo zokha ndye kakuzimphweteka🙌🙌🙌😍😘

Address

Kasungu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when HOHO TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category