Ba Moja

Ba Moja Young Ideas Investment.

Supporting local/small businesses in rural areas in Malawi Information provision Business links,Finance Management, Marketing and Grants, Creation of Content to Educate and entertain.

22/09/2025

Masamu ake siovuta.
Set agoal
Plan
Stay focused
Ulendo uyambike basi, taking a risk today apo bii! Get set to settle for the ordinary.

22/09/2025

Morning:
Be positive about today, say lero tiyesanso even dzuro zinavuta koma lero tipusha than dzuro. Wake up and gooooooo

21/09/2025

Business idea at the right time.

Congratulations to Spanner Malawi  chikwama wachitola over 18 mita.Now guys pali ena omwe mumaseka hustle ya mfanayu kom...
21/09/2025

Congratulations to Spanner Malawi chikwama wachitola over 18 mita.
Now guys pali ena omwe mumaseka hustle ya mfanayu koma dziwani kuti ku pusha ndi kupusha basi bola ngati sukuchita zolakwika.

Chithuzi chinacho ndi cha mkulu wina yemwe a matsitsa mpweya pa stage modabwitsa nkumapeza khobidi. Let Spanner Malawi be.

tipushe basi.
Follow us today.

20/09/2025

Haye haye

18/09/2025

Tiyeni tipushe gin osatopa

17/09/2025

Keep on pushing palibe boma lizatipatse zaulele zosintha miyoyo yathu, kochepa komwe kalipoko kankha Gie.

17/09/2025

Elections and the Youth......

Apa wachinyamata kungo usidwa. In Mangochi ati kufuna kukasokoneza zisankho other two asweka.
16/09/2025

Apa wachinyamata kungo usidwa. In Mangochi ati kufuna kukasokoneza zisankho other two asweka.

16/09/2025

Leroli koma kuli busy, wachinyamata ukukavotera kuti. Ine ndi Mzimba Central.

15/09/2025

Usiku wa bwino mawa kavoteni

15/09/2025

Address

Lilongwe Area 18

Opening Hours

01:00 - 12:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ba Moja posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share