Brave G Banda

Brave G Banda Malawi congress party

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚uyu analodza malawi ndiwankulu matako Escom ya Dpp nayo sikudziwa chomwe chikuzimitsa magetsi... By the way Saidi p...
14/09/2026

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚uyu analodza malawi ndiwankulu matako Escom ya Dpp nayo sikudziwa chomwe chikuzimitsa magetsi... By the way Saidi pansana pako ndiwe amene ukusokoneza dziko lino kuli mavuto kunjaku tisamanvele iweo Unatseka njila zonse zomwe president amapezela nkhani pa ground unamupanga hack president ali mkhwapa mwako munthu onyasa moyo iwe.

14/09/2026

Kunali nkumano kunyumba yachimfumu nduna zina zinakapempha chilolezo kwa APM kuti apange zoti amuchotse jane ansah ndipo asankha kale munthu oti aipititse ku parliament kuti aphungu akambilane thats why jane Ansah sanaitanidwe kunkumano wa nduna.

Nkhono za Dpp zagundikatu aaaaaa kkkkkk mulibe zochita
14/09/2026

Nkhono za Dpp zagundikatu aaaaaa kkkkkk mulibe zochita

14/09/2026

Dziko la anthu osayamika limalamulidwa ndi asatana malawi ndidziko la anthu osayamika mpake pano tikuona gehena

13/09/2026

Sindinaone team yawuchitsilu ngat manchester united very useless team kumafa ndi team yolandila red card zauchitsilu

Kod anthu inu izi mmachotsa bwanjj
13/09/2026

Kod anthu inu izi mmachotsa bwanjj

Awa ndi akuti ndi vikitala misomali awowa afotokoza monveka bwino kuti Ku Dpp kuli katangale ndalama zubadwa alankhula i...
13/09/2026

Awa ndi akuti ndi vikitala misomali awowa afotokoza monveka bwino kuti Ku Dpp kuli katangale ndalama zubadwa alankhula izi dzulo ku thyolo

12/09/2026

Ku inbox kwanga kuli mamesseges more than 1000 aMalawi kulila ati tinapanga chibwana kuvotela dpp

11/09/2026

Uyu samayenela kumwalira fast amafunika adzaone mbwelela zili lero boma lili mmanja mwama monkeys sakudziwa kuti zimatani.

11/09/2026

Dpp yayamba kunyengelela ma mp a Mcp kuti achotse speaker paudindo wake ndipo amati aliyese apatsidwa 5million koma chipani chokonda dziko cha mcp chakana mwantogalu.. Pano akusakasaka njila ina yopangila convice ma mp kufuna kuonjezela ndalama ati suleman achotsedwe.

Address

Lilongwe Area 18

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Brave G Banda posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share